Khalidwe la a Malawi ndilowola – Mutharika
Lolemba, mtsogoleri wa dziko lino, Pulofesa Peter Mutharika, anasambwaza a Malawi. Iye anati ndi okhumudwa ndi anthu a dziko lino kamba koti ali ndikhalidwe lonunkha. A Mutharika anakamba izi pamene anali pankumano ku Mangochi ndi… ...