Apolisi apulumutsa Gogo ku Thyolo
Chipwilikiti chinabuka m’mudzi mwa Molande, Mfumu yaikulu Nchilamwera m'boma la Thyolo komwe apolisi alandisa gogo wina m’manja mwa anthu okwiya omwe amafuna kumupha pomuganizira kuti ndi mfiti. Chinautsa mapiri pa chigwa nchakuti la Mulungu pa… ...