Siyani nkhanza kwa amai – nduna iwuza otsogolera zionetsero
Nduna yowona kuti pasamakhale kusiyana pakati pa amayi ndi abambo pa ntchito, a Mary Navitcha, apempha kuti azitsogoleri a mabungwe omenyera ufulu wa anthu mdziko muno asiye kuchitira nkhanza azimayi. Mai Navitcha amalankhula izi pazionetsero… ...