Inu a kumpoto, iwalani za u President – yatelo DPP
Ngati muli a chigawo cha kumpoto ndiye mumakhumba kukhala President ndiye kuti ndinu munthu wa chibwana kwambiri. Malinga ndi mlembi wamkulu wa chipani cha DPP Mayi Grezzeder Jeffrey wa Jeffrey, palibe munthu wa kumpoto angakwanitse… ...