Inu a kumpoto, iwalani za u President – yatelo DPP

497

Ngati muli a chigawo cha kumpoto ndiye mumakhumba kukhala President ndiye kuti ndinu munthu wa chibwana kwambiri.

Greselder Jeffrey

Greselder Jeffrey: Akuti ku mpoto sikuzatuluka mtsogoleri wa dziko.

Malinga ndi mlembi wamkulu wa chipani cha DPP  Mayi Grezzeder Jeffrey wa Jeffrey, palibe munthu wa kumpoto angakwanitse kukhala mtsogoleri wa dziko lino.

Mayi Jeffrey anena izi pa msonkhano umene anachititsa.

Pa msonkhanowo Mayi Jeffrey anapezelapo danga lothila ukali Bambo Frank Mwenifumbo amene alowa chipani cha AFORD.

“A Mwenifumbo ndiye ndi omvetsa manyazi, nanga munthu wamkulu lero ndi kumapita ku AFORD?” analankhula motero.

“Ife a DPP tinawauza abwele mbali yathu, koma iwo kukana ndi kupita ku AFORD. Kodi ngati anakanika u President ku AFORD a Chakufwa Chihana, a Mwenifumbo angautenge?” iwo ananyogodola.

Pofuna kuonjeza chipongwe, Mayi Jeffrey anauza anthu kuti chigawo cha kumpoto sichingakwanitse kutulutsa President chifukwa kuli anthu ochepa.

Share.

497 Comments

 1. Paja mudabadwa ngat nchenche mmavutitsa anzanu mukayandikana ndikufa,upresident mwautenga ngat umfumu wa kwamanu et.chot udziwe amalawi tidaleka kusekelela zopusa coz umpawi udatikonda.zoona mbewu tizigulidwa motchipa pamene katundu ndiokwela tingatukuke bwanj

 2. Kayini Matthew Major you should not be my friend from now on. Iam not associated with people of tribalism and nepotism or regionalism.Iam not from the north but you have handled the brothers well. Iam a Senga from central region mchinji

 3. Zonsezi tamva chabwino, kuthetsa nkhani apapa anthu a pa kaya ingolimbikirani kubabana so that your population can surpass that of the central and south basitu in 20 years time wanu wanu prezdente uyo!!

 4. ine wakumpoto. iwe walemba na uyo wayowoyanga mose vondele pera ntchigukwa uli pera uzulana kumpto mwavindere imweee? nokumuchema mabus yoyoyoyo yayi tikachilireko njala tionesanenge nxt season

 5. nanuso atumbuka muziwatibula alomwe amenewa akabwela Ku chiputula muwa sake mmiska alimo alomwe azipita Ku mulanje akudelela mtundu was school pa Malawi

 6. No problem and there is no one need to be a president in Mpoto because this country is too poor and there is unemployment so we don’t need a president from our side Peter he’s the one who make Malawi to be poor and Malawi will never get rich because Chewa’s tribe they taking themselves like they know everything but they fool ,,, even u can say people from Mpoto they are foreigners in Malawi we don’t care

 7. You people amuse and amaze me, coz go in offices you will find that the northerners you insult every time are the big bosses, and the southerners you praise every time are house maids, garden boys and gards. They even come to north kuzalimitsa as tenants , shame on you people who always criticize northerners

 8. God’s ways is totally different from our ways. Analipotu anzanu, de same position ur holding, Secretary General of dat same party, ( RIP ) nawo ankayankhula motumbwa. Anwae akukhululukileni Mulungu for regarding some ov His creatures inferior.

 9. The word tribalism…it’s very bad for our African continent specifically Malawi….this notion “tribe”…is a racist term with a very bad negative connotation….

  Out of this word civil walls emerge…& we all know the consequences….

  We are all Malawians…that’s that…nothing else…!!

 10. Awo ndimaganizo aumwana and achikunja. Adziwe kuti Aizilayeli kanali kamtundu kakang’ono mukati mwa Aiguputo ndipo amatengedwa ngati akapolo koma mulungu anamva kulila kwao and anawaombola modabwisa Nanga anthu akumupoto sangawaombole akafuna Mulunguyo? THINK B4 U SPEAK.

 11. Mpoto everyone is president by himself because we are fighting for ourselves and we don’t have much time to complain about that your president peter is pusy!! Musalimbane ndi mpoto zathu zinayera kale we can’t west time for nonsense timadzimenyera tokha ife aliyetse ndi president munyumba mwake

 12. Pepani pepani amalawi nonse mwaponya maganizo anu kumpoto kummwera pakati tonse ndiamozi km ngati sitisamala tionongana tokhatokha atolankhani ndiwo amabweresa mkhondo nziko ineyo sindikukhulupila KT wanzeru angamanene motero kodi maesa a kumpoto mwakwatira kummwera akummweranso chimozimozi ndiye chotuluka mmenemo mayesa ndiye mmalawiyo tisakhale tikukokana tiyeni timange ziko lathu maofesi ambiri muli akunorth ngati zinthu zikuoningeka ndionse amene akutuzunza osati alomwe chisanzo minisitala wazachuma chuma chikamaonongeka asasamala ndani

 13. AMALAWI, ATATE NDI AMAI: TAONANI, Kusagwilizana kuja anthuni m’mene kukufukulira m’nyozo pakati pa AMALAWI: AMAI alankhula nkhani’yi pa msonkhano wa DPP sadalankhule bwino. N’theladi ndizija amanena kuti UTSOGOLERI wopatsa ana ang’ono umaipila pomwepa! AMA kodi anthu akugwila ntchito M’BOMA ONSE NDI AKUMWERA POTI UTSOGOLERI UFUMILA KU MWERA? NGATI AKUMPOTO ALIMO M’BOMA NDI M’MENE MWALALATILAMU N’KUTI UTUMIKI WAO UKHALA WOLONGOSOKA? CHIPANI CHA DPP CHIFUNA CHITUKUKO KOMATU INU MWAIPHATU APA DPP IKUONA CHIFUKWA CHA CHIBWANA MWAUPELEKA ULEMELERO WONSE TSONO KU MCP! Ndi zoonadi kuti mkazi opusa amagwetsa (kupasula) nyumba yake ndi manja akedi? Kodi kumpoto kulibe A DPP? Ndiye ndi mau mwalankhulao ALOWELA KUTI A DPP KU MPOTO NGAKHALE ALI OCHEPA IN POPULATION? AMA munthu aliyense ali ndi UFULU WOSANKHA CHIPANI CHIMENE WAONAMO MFUNDO ZOTHANDIZA DZIKO LAKE! NDI CHIFUKWA AMALAWI ADASANKHA ULAMULIRO WAZIPANI ZAMBIRI!!

  • CHIHANA mukumunenayo AMAI adali mwamuna ogona ku khomo kosatseka! Kodi inu simwabadwa NGWAZI ITAMWALIRA! AMAI pamafunika m’tsogoleri womuchotsa NGWAZI pa mpando! Ndiye m’tsogoleri’yo adali CHAKUFWA CHIHANA WAKU MPOTO!! AMA mwauona udindo muli nawowo n’theladi ndi CHAKUFWA CHIHANA, unyolo ataubvala CHIHANA m’manja kuti inu AMA PAMODZI NDI ATSOGOLERI ANZANU MUDZITUKWANA MAKOLO ACHIHANA PAMODZI NDI ABALE AKE A CHIHANA! KODI AMENE WABVALA UNYOLO NDI SADAUBVALE M’TSOGOLERI NDANI? NDIKUDZIWA KUTI A DPP AKUPHUNZITSANI MALANKHULIDWE ABWINO A NDALE ZA CHI MALAWI!! ANTHUNI INE ndakhala ndikulira pampano kuti ndi atsogoleri otani a Zipani zonse M’MALAWI osadzudzula ana ao pazatsankho,m’nyozo anthu akukamba! MPAKA MU NYUMBA YA MALAMULO PALIBE M’TSOGOLERI ADALANKHULAPO ZOKHAZIKITSA PAMODZI MTUNDU WA MALAWI!! KODI CHIANI?? AKULU AKALE ADATI,”M’TSINJE WA TINKANENA UDATHELA M’SIIZI!! ZACHISONI MALAWI!!!

 14. Dziko lathu kodi mukufuna tsiku limodzi tizakhale ngati othawa ngondo? zatikwana chifukwa idzafika nthawi adzawina munthu wochokela kuno ku mpoto muzalephela kuvomeleza

 15. Ok chabwino poti mwanena zo sankhana mitundu, ndeno tikupempheni kuti ngati mwapezako wakumpoto uko mnthamangiseni, ifenso tikuthamangisa anu kuno kwathu kumpoto amene amativunira tea pa kavuzi estate, chombe, vizara ruber.muzitenga ngati DPP ndiyapakhomo panu ngati kumvekana ufumu , anthu a umve inu malawi yonseyi katengeni komwe ndi kwa umve ndi kumwerako assaa kunyela podwera. Ngati mukufuna kuti DPP ithere panjira tangonenani muwasatire achimwe anu ndi kharidwe lonyasalo kupusa peee.

 16. a wise northerner can no longer admirer to rule already plundered, violated, abused, torn,a shame and poor nation like Malawi,it is cursed for denying good people from north and allowed selfish and thieves to rule

 17. Malawi is one and Malawians are one, and what so ever anybody can say Malawi will remain one. And I don’t think there is anybody who can divide it. Gentlemen, why should we been busy dividing one family instead of taking time defending our lake along Tanzania-Malawi boundaries? Let’s think twice leave the citizens of Malawi in peace. We all knows that contesting presidents comes from any regions Malawi and from any district which shows that there is no ristriction of presidents in regions.

 18. Panyo pinu imwi mukamba nkhani zo mweni mavi pamoyu chupiti zinu agalu imwi ake kumupotu tewanthu akusambila pee isi pamavi pinu mosi a dpp mukuchenje bweka limu mweni ndaliso zapamataku mwanimwazadi ndi ndali zinu zo zaugalu

 19. Its true kumpoto kuno sikungachoke president analephera chakufwa thom chihana basi palibenso wina kwasara zitsilu za anthu monga phungu wa rumphi east komanso akamuzu chiwambo ndi anthu oti olo titawapasa mwayi sangalamulire

 20. Iwe Peter naweso uyiwale kuti uzawinaso Malawi wakulephera chomwe umatha ndi tsankho basi nanga zinka number 1 koma mmutu mamina okhaokha ndimadziwa kuti ukangonyera mwana NDE kuti ukudwalaso. Mind you panali mkulu wako apo koma alikuti.

 21. Let’s go back to our Bibles, these are signs of the end, so don’t be surprised, just proceed with hard prayers we have got our own King of the kings the one who is about to come for the saints ( JESUS CHRIST)

 22. Go to hell with ur poor leadership, don’t u know that you are the worst president than ever before, am proud to be northerner and am proud to be Tonga by tribe finally am proud to be a poor Malawian just becoz of you , all northerners who belongs to DPP you are idiots

 23. Ha! Mbuli zawanthu ndichifukwa chake MLUNGU, akufuna kupeleka chigawo chakumpoto kudziko la TANZANIA! ndadziwa sopano mtima anthu akumpoto yankho lanu lafika ndipo mkwiyo wamlungu ukubwera kwaonse odana nanu khulupirani zimenezi.

 24. I am a Lhomwe but anzathu a DPP wa kunena mosapsatila ngopanda ulemu, ankhanza, amtudzu ,akuba komanso opanda ngakatangale. #1_less_vote_4_DPP

 25. Koma nde a DPP mwafikapo, koma musaiwale kuti anthu amene mukuwanyoza lero mawa azakhala mabwana anu
  Nyozani mumene munganozere ife akumpoto sitifa aii,simunayambe inu a DPP and ife akumpoto sitikuteketseka nanu thawi ndiyanu iyiii

 26. 4kolu ngati president akumasala chocho pomwe even mpoto yomweyo yinam votera umunthu ulipo? Zidwaniko zomwezo Ana anjoka enu, kaya kuli president kaya kulibe czikuziwidwa nikomwe, am from mpoto and I hate if sameone is saying president of malawi or MP, zimazagwada pa nthawi yoti tivifake pampando Kuli efe olirafe, koma vikango kwerapo pamenepo vayamba kukamba vaupuwa, nyero zanu nonse Ana anjoka enu

 27. You can’t talk like that while you have members of that region if those people reunite and take northern region as their country like Wandale .Plz avoid words of division

 28. koma zikoli la Malawi pomwe lizzakhale ndi president wakumpoto lizachita bwino kwambiri inu zakukanikani bwana .malawi yose mavoti anu ndi five hundred yokha poti mumaziwa kuba muzabaso. koma mpoto yilibe polobulemu

 29. How can someone called a politician say like that? Go to hell politicians with their brain in the nose.Some countries that experienced wars are doing better than our country so is there anything we can show off apart from stealing government money??? Tribalism, regionalism and nepotism are the things killing this country .Happier are the eyes that sleep….

 30. This’ posted as an opportunity to make DPP unpopular in northen region.the fact that its the least populated region is true and that we have unpopular politicians.dividing malawi can’t be asolution to this challenge but abolish the quota system in education will help us in alot since we’ll still have such leaders in future but education is the best.what we should know is that we are not supposed to be influenced by any politician on these grievancies because these guys also contribute alot to weaken us.

 31. Am from Thyolo but i dont support this people,but what i hurt inu anthu akumpoto ndiamenenso mumasapota ndikuvotera anthu amenewa,moti 2019 mudzawavoteranso adzikulalatirani..simupanga support anthu akwanu and i dont know why ndizimenezotu….

 32. northerners are independent we don’t rely on handouts like southerners shame on you, don’t come here kudzalima fodya matenant athu inu what do you benefit from presidency we are much better than you amene mukudzitamandira inu mu tumbuka sazatheka paliponse alipo from capital hill to grass root kkkkkkk ubooka m’ mimba wekha

 33. Mulungu sataya wake don’t forget that ziko la Malawi osalitenga ngati munabwadwa nalo kubere kwamayi any eti komaso anthu akupoto osatitenga ngati ndife osarira ayi amene anena mawuwo ndichisiru kufunika kumupsa soap kuti achape mukamwa mwake mwina angaphuzire kuremekeza mutu wachimarawi

 34. Kkkkkkk, Dpp Stop Making Noise, Munthu Oziwa Kumenya Xaima Pachulu Kumaziyamikila Yekha, We Dont Care Wht U Are Xaing Time Will Come Where By We Wil Be Free Just Wait, Ku Vutika Kuli Ndimalile Remember Mulungu Xanga Lenge Munthu Kt Iza Vutika, Watch Out Ndi Prezdent Wanu A dpp Xazakhala Muyaya, Tel Mi Whr Is Bingu??? Osamayankhula Ngat Akudulan Mutu,

 35. Please secretary,this is not a good view because you as people of center and south are not the owner of the country. Who are you to talk about it and where were you when were alive, think about. Things are changing as you were nothing at Banda government don’t still hiding angels of God as they are born therefore they have certain commitments to the country. Even the colony are no longer in Malawi, please think,think and keep thinking.

 36. I hail from Ntcheu but this is one in a million posts that deserves no room in our society and country…..The fact that one comes from any of the region or district doesn’t suffice the reason why he/she must looked at as adversary or foe,we use one demarcated map,one flag and this,signify that we are all Malawinians.Remember,Malawi is poor but rich in being a country that flourishes in peace,unity and tolerances hence,we will ever distaste those conceited and disintergrating obsession nartured in one or another way by any party or leader.DPP must take heed and refrain from proving anger among Malawins but rather strive to appease Malawians at large.Remember,an ear that doesn’t listen,accompanies the beheaded head to the grave

 37. Akumpotowo ndiye kuti si a Malawi? Izi ndichifukwa chake timati tikhale ndi colonies tiike maboundary akumpoto adzionere okha nawonso aku Lower Shire adzionere okha.madera tatchulawa akusalidwa kwambiri ndi maboma a democracy alipo lerowa.Honourable Chakuamba was once elected by the people of this country to be the president but because of tribalism justice paved way to injustice.No matter where one comes from but as long as he has a vision to uplift Malawi we can give him a chance but our choices brings wrath upon God when it reaches to extent choosing Peter Mtharika to become the president now he isgerminating feathers of flying high with corruption and wickedness on everything

 38. DPP should not forget that palibe wamuyaya and among you there is no any other character for presidency if Peter goes apo ndiye tiziuzana Chilungamo ndipo musayiware kuti ngakhale Pitalayo siwamuyaya. Akadzangochoka ameneyo basi uchitsiru wanu onse udzaonekera poyera, inu ndamene mukuononga chilengedwe pomaberekana ngati nyelere kufuna kukawina ma vote? Stop making those foolish remarks we are all Malawians and you will be disappointed one day to be ruled by a northerner

 39. Bwanji mumadana ndiabalenga akumpoto mwaiwala kuti kaufulu mulinako lero anayambisa ndi chakufa chihana wakumpoto inu akum’mwela ndi pakati munali kuti ? Mwaswera nzanu atayambisa kale kuigwedeza mcp yankhaza one day is one-day akumpoto azalamula dziko la Malawi

 40. #Chirambo!
  May be you should know sometimes why women gets promoted into top positions in any workplace.
  -Very few it has to do with a proper promotion because of the experience and skills she has for the job.
  -Most women they get promoted by using their “gooners” and nothing else-No experience, No skills [may be she has bedroom skills only]
  Seduce the boss of the company etc and all over sudden she is promoted to the top position.
  And when this five star slag gets to the top position, she behaves like a dinosaur.
  Remember she didn’t went to school!
  A person who went to school can’t behave like this Jeffrey woman of Dpp.

 41. if this shit is true i dont realy give a damn and i know that there r pple who think that way ndipo chikanakhala chipani chenicheni kapena dziko lenileni i wud’ve been worried bt its a shit of a country and u can hav it.time is coming that the north will b a country on its own even if it means that blood will b spilt, mark my words i know damn well wat i’m talkin about!

 42. Ok fine tamva!!but u should know that ife akumpoto ndiamene tikutukula dziko la malawi poti palibe chigawo chomwe chili ndi anthu ophunzira ambiri kuposa kuno kumpoto,ma office ambiri akumpoto ndi amene tikuyendetsa,Nduna ya za chuma ndiyochokera kuti?mpira umene ndife akuno kumpoto amene tili ndi osewera ochuluka,osataya nthawi ndikukhala anthu osakhana zigawo zochokera ai,mtima umenewo sitingapite nawo pa tsogolo ngati dziko!!!

 43. Kkkkk zaziiii kusowa zokamba.Mavuto ali thoo kumwera kwanuko komwe kuli President ,ndeno mutiuza chani chanzeru? Pitani kwawo kwa President anuwo mkaone anthu momwe akuvutikila ku Thyolo bola kumpoto .Osatinamiza ndzosagwila mutuzo.Mudzakhumudwa Mulungu simunthu . Get out

 44. Zingoona kuchitika pa ndale apa. Enanu mumangolankhula ndale muziziwa kuti ndikupikitsana. Yes, DPP can say that because it has confidence. So we dont know but what I feel sibwino anthu a ku mpoto kuchita mantha ayi ngati nkoyenera kupikisana nkoyenera Mada we see you all as Malawians there is no foreigner in Mpoto but if we have anyone who can stand as a president well its fyn, we can do that. Anthu kwawo nkuyankhula amafuna awone reaction ya wanthu basi

 45. The problem we have as Malawians is that the majority is from Southern and they vote for wrong people. At the end of the day we suffer as a nation.Wake up Southern people!!! and unite with Northern region.When it comes to voting and eliminate those corrupt people and lets benefit as a nation.begging until when???? Let’s make good choice who to lead our country!!! and be hard working and push our country forward!!!

 46. I don’t see any problem with this but keep in mind mpoto bukhu ndikawawa andso sitifuna zolimbana ndimunthu komaso Dpp ikhale konko komwe inachokera bwanji? Gwenembe wachabechabe

 47. How should I describe these DPPs I’m sorry I will use stupid DPP when describing them, how many leaders do you have in DPP from north if u are saying that then notherners let’s stand together to fight so that we become a nation on our own we should not be part of Malawi

 48. Inuyo akunmwera u pressident ndiwanu koma mukupangapo chani chotukula ziko lanu umphawi uli thooo ndichifukwa chake achinyamata akumapita ku maiko ena kuka funa ndrama mwalamulila kangat kaziko aka simungamasileko ma neibhors akutukuka ponpa apa inu mukungokakamila zinthu zaziiiii mukhale ndi upressident umphawi suzantha muno malawi simungasintheko ai koma kakaka uku anthu mukuvutika palinzeru

 49. Tonse ndife a Malawi.DPP yabadwa liti kuti aziyankhula motumbwa chonchi? Let’s unite and develope our be loved Malawi. Tisachedwe ndi kukumbana mitundu.Wake up Malawi

 50. oil malasha forest lake are building north Malawi its not high population which can build the country when you got alot of population there’s high problem of tribalism

  only strong minded people will understand this

  northerner

 51. This can’t be true.
  I am a Southerner, Phalombe to be so specific. With parents (late) of which one was from Phalombe and the other from Nsanje. They taught us to be associated with others regardless of where one was is com

 52. People, this is not true, examine the text before posting your responses because from the look of it, the grammar of the text shows that the writer is not sure of his own writing, he wants to see how we people can react to that, he wants to play with our minds especially those who rush to comment without thinking dont trust any post from any page, this is why other ignorant people see our ignorance and conclude and label us as opusa, wise up wanyane

  • Mayaz, we should stop dancing to every beat, akangot mwakut ife eeeeeh aaayi aaawwaaaaa ichi awa icho ife paja izi, mmmmh sometimes i laugh not because i find it funny but, nkango abangulabangula sugwira nyama, lets fetch for a gvt that will do the good we want and promote that than kutha mpweya by discrediting amene akuzichita discredit okha kale. Koma ndiofoira mkuluyo

 53. In that case then do u ever come n campaign here coz it shows kuti u just use us the Northerners so I would like u DPP to distance yourself for begging us to vote for u , agalu inu

 54. Kkkkkk zazii zomwe amadya ma President anuwo simmadya nawo ndikunyumba kwanu sakuku ziwa Ali pheeee ndiana awo nde inu kuvutika ndi ukazitape basi sukuluso njeee iyaaa zausilu

 55. DPP mudziwe kuti kuli Mulungu ndipo bible likuti chitsilu chimati kulibe Mulungu nde zomwe mukuyankhulazi mzauchitsilu; mukudzitenga ngati inu eni dziko? Mwapha miyoyo pofuna ziwalo mulamuliro wanu? Mwaba chuma chochuluka chingati? Mukuona Mulungu sakukuonani? The way you are speaking ndinu dzitsiru.

 56. Tikamphalilani tikukhumba u ptesdent kuno ake tikumanya tingapikisana namwe yayi mli wanandi ndi family imoza wathu 15 na wathu wakuti family imoza 5 mnga yana kkkkk kweni namwe mganizenge malo moti mganizenge vakuti mngapa uli kuti kuchulukana mleke mbwe mli bzy kulimnana na taba tumbuka

 57. chonchi kumeneku kukhale kuyankhula kwa munthu oti anapatsidwa udindo kuti dziko lidzimva ??? chipani cha dpp khalidwe ili ndi lawo anayamba ndi bingu ndi achaponda lero adakapitilizabe nawoso awa mukuti agilizidawa mwina akufuna kutchuka basi imeneyi ikhale fundo yoyankhula gulu likumvele kupanda mzeru ndiye kwakula basi

  • man sizowona lero lino munthu wa mzeru angamakwele pa chulu kumanyoza anthu achigawo cha kumputo ayi ngati zili zifukwa za ndale osamusiya munthu anasankha ekha kukatumikila aford koma nanga imeneyo ikhale nkhani yoti aliyese wakumpoto asamayembekezele upresident aaaaa kuteloko gilizida adabadwa ali mp ???? umbuli si school yokha ndithu

 58. President amakhala munthu m’modzi pa 5 yrs while u boss ma company ambiri timalamulira ndife ngakhale m’bomamo maudindo akuluakulu ndi athu akumwera wanu ndi utenanti olima fodya Ku mzimba. ngakhale company ya Illove sugar singayerekeze kuzatenga udula mzimbe kumpoto never

 59. Moyo Oipa, Opasula. Anthu Aku Mpoto Ayenera Kuganiza Mofatsa Ndi Kusankha Wanthu Amene Azawalemekeze Osati Wanthu Amene Amafuna Kuwagwiritsa Ntchito Ngati Zikolopa. Wina Anayankhulanso Mawu Amwano Ngati Omwewa Ponena Kuti Chipani Chawo Sichingadalire Wanthu Aku Mpoto Pa Chisankho. Wina Mpoto Think Twice.

 60. Inde zilamulani bomalo komaso ifeso tikudalira inuyo akumwera ngati anthu ozalima ganyu mminda yathu ku Mpoto. Ndiye pamenepo pakuwoneseratu kuti ndinu anthu opanda zeru chifukwa chake mukasankhana nokhanokha anthu Osalira inu.

 61. Kkkkkk Dpp Wakukanikani Utsogoleri M’malo Moti Muzikamba Zamabvuto Alidziko Muno Busy Kukamba Zakumpoto .President Ali Ngati Mai,ndiye Sizingatseke Mwana Obala Iwe Yemwe Ndikumamutoza Imeneyo Timati Ndi Kusoweka Chikondi Kaya Mwina Poti Sadakusankheni Ndi Anthu Koma Maganizo Awanthu Mukawava 2019 Mukachite Kubelansotu Shame On You

 62. kwaine ndikoyamba kumva chipan cholamula chikuyakhula zimenezi, voto ndilot amalawi tili ndidyela muthu oti wakulila maiko akunja kungobwela Kuno bas ankhale tsogoleli ndi izi lero wayambaso kutinyoza mmmh akadanyoza ife achigawo chapakati ndithu akadafa infa yowawa

 63. Some things are better left unsaid. You won’t regret for the words you never say . You can’t reverse what has been uttered. Dpp will be hunted by this address !!!

  • akulu thamangani mukadzudzule munthu amene wayankhula mau amenea osati awa amene apanga post nkhani ayi m’mesa awa akunena zomwe zayankhulidwa ndiye alakwa chiyani

 64. Mau awa ayankhulidwa ndithu dzili kwa anthu akumpotowo kudzasankha mwanzeru popeleka vote kwa munthu amene satha mau kuiwala zoti vote yathu idzafunika.Kodi anthu akumwera ndipakati mudzanyodza anthu akumpoto mpaka liti?Timayamikira Patricia kaliyati dzana dzanali pothandidza team ya chitipa united idzi ndizimene timayembekedzera wakumpoto,wakumwera komanso pakati ndife amodzi funso ndilakuti kodi tidzakhalira kunyodzana mpaka liti?Chifukwa chadyera nditindalama tochepa tomwe amatipatipatsa nthawi ya campaign timaiwala chitonzo chonse ndikuvoteranso Dpp kodi anthu akumpoto tidzanyozedwa mpaka liti?Akatipatsa ndalamazo tiyeni tilandire koma nthawi yovota tiyeni tiwaonetse chimbenene ulendo uno tatonzedwa mokwana asaah

 65. hahahahahah munakavota nokha lero izi akusasani alomwe sayamika bola dyomba bakili anazungulira malawi yonse kuyendera anthu panalibe ndi tsiku limodzi lomwe ananyoza mtundu mu dziko muno mbuzi imeneyi ilibe umunthu

 66. This is what happens when you put a woman on power, they behave like a dinosaur and most of them end up being kicked out of their top positions i:e former women president’s of Brazil, South Korea, Malawi, Argentina etc.
  I think this woman is a product of uhule, one of her parents was either a slag, harlot or a Jigalow.
  She doesn’t even have no idea in regards to the history of Democracy [Multiparty] in Malawi and who first brought it.
  May be she is a refugee from Congo or Burundi, please investigate her.
  We don’t have such people from the north and most especially the entire country.

 67. No problem even if the DPP see mpoto as foreigners in Malawi. Its high time we have been fighting nepotism and regionalism to end. Go on because even if some may condemn it and others will carry it on and passed to their new siblings. Its very unfortunate that northerners are insulted in many ways. If you are tired of them why cant you release them free that atleast they will have a capacity to look on themselves. On our diverse cultures we had an opportunity to come together and share what we have in common, food, dances, rituals, languages etc. Its an insane to call some body a chewa, a tumbuka or a northerner in an insult way. Yap we will not produce a president since we are not united as Malawians but we are divided by tribe. Shame on.

 68. Palibe vuto, olo mutati akumpoto siamalawi, chifukwa sindikuwona phindu ndimalawi wathuyu. Zaziiiiiiiii…….. Kadziko kochepaka uphawi uli thooo kumasankhana zoona? Kkkkkkkkkk Peter Muthalika.

 69. Iwe kulemba iwee pamozi na chakufuntha chako chi pitala icho mavi yinu mosee mulivindele chomene. Ise tikulya u president yayi, tikulya vakulya vithu. Imwe mwazgowela kupemphapempha ndimwe mukudandawula

 70. A Dpp mwatani?mukuyesa kuti ndinu a muyaya,analipo otere koma ali kuti,ndani amadziwa kuti PP mkulamulira,zitachitika zija,amkaziwa ndani kuti UDF mkulamulira boma Chihana atatchuka-amangwetuuu!!

 71. Or ku America nakoso ankalankhula mawu onyasawo kut wakuda sadzalamulila , koma inafika nthawi mpaka Obama analamulila. Kumpotoso idzakwana nthawi adzalamulila

 72. No stress alomwe abwere kuno kudzalima fodya malipiro awayilesi yapanasonic. Mtundu uyu unakakhala mbeu yachimanga ndikadangokazinga. Umphawi paMalawi chifukwa chamtundu wotembeledwa uwu. Mwana wafisi. Kuberekana ngati mbewa. Anywhere we don’t stress because mbuzi zichokera konko kubwera kudzatilimira fodya

 73. Kuyankhula koti mwakhuta uko sikwabwino
  Ndani wakumpto analamulirapo dziko lo?
  Si inu nomwe achewa,ayawo,nda lomwe mwaliononganso?
  Kazilamulirani ndikumapha abaleanuwo kwa tembwe,kwaciwere ndinjala

 74. Malawi ndi dziko la aliyense, kaya ndi ku mpoto, pakati, kaya kunvuma ndi ku mmwera komwe. kuyankhula kwanji kumeneku. Ngati DPP ikuona ngati 2019 mpatali ikuzinamiza. ngati DPP ndi ufumu, ufumu umeneu wayesedwa ndipo walephera
  nkhawa yanga ndioti mukuika alomwe onse osalakwa kuzalandila nao sankho inu mukazachoka

 75. Page iyi tisamale nao ikhonza kuyambitsa makangano ndi ziwawa. Kodi mwawafunsa a DPP kuti mumve mbali Yao kapena mwangomva kwa ena. Let us be careful with this kind of unbalanced reporting which can create enemity among peace loving Malawians.

Leave a Reply