Mbava zowombera mwini nyumba zagwidwa ku Blantyre
A bambo atatu ku Soche mu nzinda wa Blantyre, ali manja mwa apolisi kamba kowombera ndi mfuti mwini nyumba yomwe anapita kukaba. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya Soche a… ...