Bambo wafa galimoto yake itaombedwa ndi sitima
Bambo wina wa zaka 33, wafa galimoto yomwe amayendetsa momweso munali banja lake itaombedwa ndi sitima ya pa mtunda pa malo owolokera ku Machinga komwe anapita ku tchuthi. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa… ...