Madzi okhalitsa amanunkha — Chilima
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima dzulo anayankhula ndi a Malawi ku Mzuzu dzulo komwe anapereka miyambi. A Chilima anafika mu mzindawu dzulo pa ndege ndipo analandilidwa ndi chikhamu cha anthu chomwe… ...