Mu 2024 mutimva Zigege — Watero Dan Lu
Oyimba Dan Lu watsindika kunena kuti chaka chino anthu amumva Zigege ndi nyimbo zimene akonze. Dan Lu masiku ochepa apitawa adalemba pa tsamba lake la mchezo kuti "Onse amene timanenedwa kuti ndife ma Savage mafana… ...