Anthu 12 avulala pa ngozi ku Blantyre
Anthu khumi ndi awiri, avulala pangozi yomwe inachitika ku Kanjedza-Blantyre pamene minibus yomwe adakwera inalowa mbali yolakwika ndikugunda galimoto ya mtundu wa Corolla isanagunde minibus inanso. Malinga ndi Mneneri wa Polisi ya Limbe, a Aubrey… ...