Mayi Bomba anjatidwa ataba galimoto ziwiri zobweleka
Mayi wa zaka 42 ali m’manja mwa apolisi munzinda wa Lilongwe pomuganizira kuti anaba galimoto ziwiri zomwe anabwereka kenaka nkukazigwilitsa ntchito ngati chikole pokatenga ngongole ya K27 million. Foster Benjamin yemwe ndi wachiwiri kwa mneneri… ...