Joyce Banda anandikwiyila chifukwa ndinamuletsa kupititsa ‘uhule wake wa ku Lilongwe ku China – APM
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika wayambapo kumema anthu kuti azamuvotele pa chisankho chimene chikuyenela kuchitika chaka chino ndi moto ndi ukali. Pa msonkhano ongoima umene anachita ataima kwawo kwa Goliati pochokela ku sukulu ya… ...