Khwimbi la anthu m'dera la Mangerengere Mfumu yaikulu Kapalamula m'boma la Balaka lachiwiri m'mawa lidakhamukira pa nyumba ina pomwe pagwa chinthu china chodabwitsa m'maonekedwe ndipo akukhulupilira kuti chinthucho ndi ndege ya ufiti. Chinthu chodabwitsacho chomwe… ...