Mtumiki wotchuka kwambiri muno mu Africa, Shepherd Bushiri, sizinawathere bwino ku South Africa komwe akudzulidwa ndikudyedwa ndi Bambo Mboro. Iwo agonjetsedwa mu round yoyambayeniyeni pakukumana kwaoku. Mwakuti pano anthu akuti Mboro watsiya Bambo Bushiri alitapsa… ...