Bungwe lomenyera ufulu wa anthu m'dziko muno lomweso akuluakulu ake ndi omwe akutsogolera zionetsero la HRDC lalengeza kuti zionetsero ziyambilaso pa 27 mwezi uno zomwe ati zichitikira mu zipata komaso mabwalo andege a dziko lino.… ...
Articles By Archangel Nzangaya
M’modzi mwa anthu opanga ndakatulo m’dziko muno a Hudson Chamasowa apempha boma kuti lilowelerepo pa ntchito yolimbikitsa ndikutukula luso la ulakatuli. Poyankhula ndi nyuzi ino, a Chamasowa anati boma pakali pano likulephera kuvomereza luso la… ...
Wapampando wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) a Timothy Mtambo, alengeza kuti ayamba aimitsa kaye zionetsero pofuna kupereka mpata ku bwalo la milandu lomwe layamba kumva nkhani yokhudza zotsatira… ...
Malawi's Attorney General Kalekeni Kaphale has appealed to the Supreme Court against a lower court ruling on his application to have the post-election demonstrations banned. Kaphale recently applied to the High Court for the ban… ...
...apolisi abweze katundu yemwe wawonongedwa.... Wapampando wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) a Timothy Mtambo aloza chala apolisi kuti ndiwo akumayambitsa zipolowe pazionetsero zomwe zikuchitika. A Mtambo amayankhula izi… ...
M’modzi mwa anthu amalonda m’dziko muno a Leston Mulli ati ndiokhudzidwa kaamba kakusokonekela kwa ntchito za malonda chifukwa cha zionetsero m’dziko muno ndipo akambirana ndi a mabungwe kuti asiye zionetsero. A Mulli amalankhula izi pansonkhano… ...
Mkulu wagulu lachikhalidwe la Mulhakho wa Alhomwe m’dziko muno a Leston Mulli ati ndiokhumudwa kuti anthu ena akusangalala ndi imfa ya mfumu ya a Ngolongoliwa. Izi zikutsatira zomwe anthu ena pa masamba a mchezo pa… ...