Dinala Chabulika
Anthu achipembedzo cha chisilamu m'dziko muno ati iwo satenga nawo mbali pazionetsero zomwe mabungwe omenyera ufulu akonza lachinayi lino. Izi zikudza pomwe mabungwe omenyera ufulu mdziko muno akhale akupangitsa zionetsero zadziko lonse pomwe akukakamiza mkulu… ...