Pamene anthu m’dziko muno akudikira mwachidwi chigamulo cha khothi pa mlandu wa za chisankho sabata lamawa, mtsogoleri wachipani cha UTM a Saulos Chilima apempha anthu onse kusunga bata. A Chilima amayankhula izi lachinayi kulikulu lachipanichi… ...
Pamene kwatsala masiku ochepa kuti bwalo lamilandu lipeleke chigamulo pa mlandu wachisankho, bungwe la chikatolika la ECM komaso bungwe lophunzitsa anthu pazinthu zosiyanasiyana la NICE apempha anthu mdziko muno kuti asunge bata ndi mtendere. Izi… ...