Malawi24.com
Mtolankhani wa wailesi ya Ufulu ku Chikwawa wamenyedwa ndi anthu omwe sakudziwika patangotha masiku angapo ataulutsa nkhani ya mnyamata wina yemwe akudwala nthenda ya COVID-19. Kumayambiliro asabata ino wailesi ya Ufulu inaulutsa nkhani yomwe mtolankhani… ...
Malawi24.com
Ngati njira imodzi yochepetsera chiopsezo chanjala yadzaoneni makamaka kaamba kanthenda ya COVID-19, boma la Malawi lalengeza kuti liyamba kupereka thandizo kwa mabanja ovutikitsitsa m'mizinda yose yadziko lino. Izi ndimalingana ndichikalata chomwe boma latulutsa lamulungu pa… ...