Dziko la Malawi lalephera kulandira katemera wa Covid-19 wa AstraZeneca yemwe amayenera kufika mdziko muno lero. Watsimikiza za nkhaniyi ndi nduna ya zaumuyo a Khumbize Kandodo Chiponda omweso ndi wa pampando wa komoti yamrsogoleri wadziko… ...
The Malawi Congress of Trade Union (MCTU) has announced that it will hold nationwide demonstrations against the labour relations amendment bill which was passed in Parliament last week. This is according to MCTU's secretary general… ...
Boma kudzera kuunduna wazachitetezo cha mdziko lalengeza kuti kuyambira Lachiwiri sabata yamawa likhala likubweza njinga zamoto zonse zomwe linalanda. Izi ndimalinga ndi nduna ya za chitetezo chamdziko a Richard Chimwendo Banda omwe amayankhula kunyumba yamalamulo… ...
Pomwe chiwerengero cha anthu omwe akupezeka ndikachilombo ka corona chayambilaso kukwera, boma labwezeretsa zina mwaziletso zomwe pakatipa zinasiya kugwira ntchito. Izi zadziwika lachitatu masana pomwe nduna yazaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda omweso ndi mmodzi mwa… ...