The noose might be tightening on the neck of estranged minister of agriculture, George Chaponda.
Media reports indicate that officers from the Anti-Corruption Bureau and the Police have descended on the houses and offices of agriculture minister Dr. George Chaponda; Admarc CEO Foster Mulumbe and Agriculture PS Erica Maganga.
It is said that the authorities are looking for information related to the maizegate scandal which has rocked the country in recent days.
Reports further indicate that ACB and police have already conducted a search at Transglobe Limited.
Malawi24 will keep you informed on further developments.
MBAva imeneyi osayisiya misokho yathu imeneyi
Kusuta
Mbuzi imeneyi muimange
“Sindinakhuzidwe ndi zonse zinenedwazi nsanje amalawi kaduka monga momwe ndinali Ku foreign affairs anali kulankhula zambiri, kaduka! Kaduka amalawi monga inenera national anthem”
Akangomangidwa mkuluyu expect my DPP vote in 2019
Iwe ujeni iwe uyu chaponda galu wachabechabe chintima ngati nyani bwantasa, afana ofewa inu okulila muthuzi ngati mapwala
Leave chaponda alone.
Amenewa ndiwo amaipitsa boma kutisilikuyenda bwno athu mkumanyoza ena pomwe iwo ndiamene akuononga amatelo?
Shaaaa! George zitopotopo ndiye zachulukatu. Apa ndiye watheka basi. Mwina amatenga ndi kukampasira ujayu monga muja ankapangira achina Lutepo. Petty cash ya ma cadet mwina. Apa ndiye Kamlepo has been vindicated. Too much evidence.
Every dog has its day.
If you are rich you are a thief or a satanist or a killer thats the jelousy Mws
Bola Azungu omwe aja basi,achulenu Mungokhutitsa mimba zanu nokha. Mudziwiretu kuti ndi boma lanuli mukuchoka. Mai Banda bwerani mbava zija zapezeka kuno. Abwiyanu ndi amene adzakuvoteni.Kulibwinonanensondidzafe Nditanena Chakukhosi Ngati LUCIUS SOLDIER BANDA “TIME”NDUZIWA KUTI MWAPSYA MTITA, UPSYEDI ZENIZENI………..
Ankolo let mw 24 talk,they wil soon apologise for misinforming the nation
Kuyambila Peter, Chaponda, apolice, a ACB… Onse zochita zawo ndizimodzi ndiye asatipusise zonse ndi mbava pamenepa
Nde a ACB apamalawi ndi Achule bwanji? Nthawi yonseyi anali kuti? Zisiru za anthu a ACB
Boma sizithu
Anthu akuvutika inu mukuba ndalama zaboma
Lets Just Wait And C If ACB Will Finalise The Case
Ingomusowetsan Asatizuze Uyu Kafukufuku Akudyaso Ma Million Ena Asoloraso Pa Kafukufuku Ameney
Paper work
Mbuzelezga apanga anganya wo. Aziwana vigunu. Chingana angafufuza ule. Palive ndikamoza kachitikengepu po go ndagota. Today its world language day. Proud to be mtonga mchanda
moshelihwa a mkandawire.Good that u have remainded me on this language day
Chitumbuka
ada bwana ndaonga, kumbi muja pani? so ise nase ndise watumbuka wa ku RU.Tikayowoya kuti boma ili lazula na wankhungu pela,wanyake wabisama kweni misana yili pamtunda yikuonekera!
Mwinaso abwanawa akudziwapo kanthu then y he is not saying anything
that ‘s throu
zuvuta kwabasi
Nothing serious will come out of that..they just want to fool us
am looking forward up the end just fire him out
2 let kungofuna kutitseka pakamwa anthuwa ndiamodzi
This is jst the same as having brai on the fucken candle. The fucken police and A C B they mst fucken wake up yeses stop fooling us oky.
https://www.facebook.com/drchaponda/
tool late zinthu waotcha kale,why acting this time? Fire him from his ministrial position
Chaponda the best way is to hang ur self man bcoz the hardness of the fire is growing bigger instead of ceasing ! If u r doing things in the darkness u must know that theres a light next to the darkness
They just want to fool us !
This is total madness, Straight out of black mirror, where were you all this time ACB and police officer? his office is already cleaned up and your busy fooling us.
ukulira chani? koma office yathu atimangire ndimisonkho yathu imene ija.
It’s too late
The maybe that there was government departments not utilized being an irregularity and corrupt intent of Chapobda.
Reality it NO MONEY was lost or stolen because Zambia did not supply the contracted maize as requested in October and before the deadline in December.
Any charges will be thrown own as no crime or theft took place possibly the allegations of conspiracy only,
Nothing will happen.
Akanakhala mphawi mutamumanga kale ñđiķumafufuza bwino
Amalawi ndife atulo amulekelela chapondayo tym yonseyo ask Dausi mesa amati choponda alive case period yonseyi sanawononge umboni? Ndife ogona amalawi tonse
Mavuto tili nawo a Malawi, Kutiphimba mmaso kumeneko, mwakhwana.
Bola asawaphenso a ACB wo mmmmm,dpp gvt
Bola asawaphenso a ACB wo mmmmm,dpp gvt
Bola asawaphenso a ACB wo mmmmm,dpp gvt
Bola asawaphenso a ACB wo mmmmm,dpp gvt
He has burnt already his office,where have you been ACB???
I’d Rather Wait And See!!! Who Gave Them Teeth?!!!
Nzongotiphimba kumaso izo mfuna mnamize ndani? Mlandu Mesa mnaweruzana kale kuti imadya pomwe aimangilira
APA ndikuthamangisa gulo mchere uli mmanja, wayenda chipindu njobvu zatchola kale zapita
Kkkkkk Tiyenayen Ameyu
kkkkkkk
Which office? I thought his office was burnt? U waited this long so that his dirty plans to conceal the evidence shud come to pass & then u get to fool poor Malawians that this dunderhead is innocent upon the findings of ur search or enquiries. To hell with u all
According to dpp’s radio station,Mbc,his office was not affected.
They Are Just Blindfolding Us They Know Each Other Nduna Ingamafufuzidwe Iri Pa Mpando ? Ndimaetsa Akanaichosa Kaye To Pave Way For Smooth Investigation THIS IS FAKE
Vuto ndife obeledwafe ,tikulolera bwanji ndalama zathu kupita choncho osapangapo kanthu? wina akakubelan malaya pakaunjika wanu nde mpak kumuotcha.nanga uyu wakubelan ma million km muli phee .mphanv ndi anthu. wake up Malawians kukhala ngat mukulamulidwabe ndi azungu bwanji?
Indeed we the Malawians We hv got aproblem. What is needed is inu muli ku ma Kolegi Try to force/assure the M R A to stop correct our taxes,because mbuzi zimezi zikamva kuti M R A yatolera k400,000,000,steeling will go highier,because they will know that M R A will collect another money. ANYONGENI OKUBA ONSEWO. ACB Mfufuzeni chaponda anagula farm ku mangochi Nakapa Vge, T/ A Bwananyambi. Ndipo Ana ena aku Chanco achitako ma practicals. Akulimako Chimanga ,Soya,ndi Mpendadzuwa. “KILL HIM”
Za zii
Hi professor, please just do one respected thing, lock up this guy his accusations are quite clear. Please do this for the sake of Malawians not for political interfearance, clean up your administration clean up corruption clean up Malawi have a good day.
Amumange kumene galu ameneyu, coz mtundu wa amalawi ukuvutika ndi njra iye kungodya basi zindalama zambilimbili. Ndipo ngati pali ena awatchule nawonso akalowe
analiko azawo amkaliseweretsa dziko la malawi coz amkazitenga ngati anazamanawo malamalo, samkadziwa kuti enaso anazamanawo kuposa iwowo, he could even tell the police to wait outside the gate till the time he wakes up. koma pano alikuti? the world is almost round
kkkk mukuzembera ajawa eit, komatu ndi a arsenal anzanu hehe
eeeh, kodi adha aja ndi a arsenal?
kkkk eya ma gunners pano nawo akushautila mu ndende kuti “Wenger out” hehe
kkkkkkkkkkkk, day1 tikamuone mgunner nzathu
tiyenayeni tikufuna chilungamo chiziwike basi
Palibe chomwe angapedze ndiponso palibe chomwe chingachitike. Sitting minister moreover ndi senior komanso mkulu wa ACB anasankhidwa ndi president yemwenso sakufuna kumuchotsa Chapondayo mukuwona ngati angamupedze olakwa mwadaladala? Ndiye kutinso ngakhale mkulu wa ACB ntchito sakuyifuna. Akungokuphimbani kumaso chinyenga aphunzitsi kunamidzira ngati kuti akufufudza chonsecho palibe chomwe akuchita.
HHHHM
Mumadyera limodzi mukunamiza. ndani; apaso tiona moto wina ku ACB ndi manyumba a police
then they will found nathing, they will conclude that chaponda is innocent.
thinking that we are fools, mesa office yake inapsa? so as the info.
kkk we are not fools!
Eeish,ine kaaa kaaa tiyenayeni…
Chilungamo Chioneke Basi
Palibe phinthu angopitira kukamuthandiza kukazinga chimanga
zongotiphimba mmaso akudziwana agulu amenewa
bolani musatinyate mmaso
That’s just for show to take us away from the truth that this puzzle will never get solved and chaponda along with all those accused will never be charged nevertheless jailed.that’s the Malawi l know
Ulendoa chaponda kouluka kazatela ukatambatamba yangana ku mmawa kungakuchele
Who is fooling who ?
ok
A chaponda !! olo mutaba reserve bank yonse simungatsungulebe thupi lanu silimva madzi ndi soap kkkkkkk
Koma2 ndika handisamala pa nduna zonse za chimuna….kkkkkkk
hihihihihihi wofunika tisiye kusamba mwina nafe nkutisankha wu nduna
Bola pa menepo
kuti watani?useless
Chaponda,,chaponda,,ndatopa Ndikumva Dzina Limeneli Wamva!!!
Wht next?
Nanga Mumachedwelanji,tikufuna zenizeni
ZILIBWINO ZED
ndiyee za ziiii
tell me more!!
Zomwe timayambekeza zimenezi …
Tiuzeni zambiri.