Breaking: Police and ACB move in on Chaponda

George Chaponda

The noose might be tightening on the neck of estranged minister of agriculture, George Chaponda.

George Chaponda
The noose tightening on Chaponda’s neck

Media reports indicate that officers from the Anti-Corruption Bureau and the Police have descended on the houses and offices of agriculture minister Dr. George Chaponda; Admarc CEO Foster Mulumbe and Agriculture PS Erica Maganga.

It is said that the authorities are looking for information related to the maizegate scandal which has rocked the country in recent days.

Reports further indicate that ACB and police have already conducted a search at Transglobe Limited.

Malawi24 will keep you informed on further developments.

Advertisement

93 Comments

 1. “Sindinakhuzidwe ndi zonse zinenedwazi nsanje amalawi kaduka monga momwe ndinali Ku foreign affairs anali kulankhula zambiri, kaduka! Kaduka amalawi monga inenera national anthem”

  Akangomangidwa mkuluyu expect my DPP vote in 2019

 2. Shaaaa! George zitopotopo ndiye zachulukatu. Apa ndiye watheka basi. Mwina amatenga ndi kukampasira ujayu monga muja ankapangira achina Lutepo. Petty cash ya ma cadet mwina. Apa ndiye Kamlepo has been vindicated. Too much evidence.

 3. Bola Azungu omwe aja basi,achulenu Mungokhutitsa mimba zanu nokha. Mudziwiretu kuti ndi boma lanuli mukuchoka. Mai Banda bwerani mbava zija zapezeka kuno. Abwiyanu ndi amene adzakuvoteni.Kulibwinonanensondidzafe Nditanena Chakukhosi Ngati LUCIUS SOLDIER BANDA “TIME”NDUZIWA KUTI MWAPSYA MTITA, UPSYEDI ZENIZENI………..

 4. Mbuzelezga apanga anganya wo. Aziwana vigunu. Chingana angafufuza ule. Palive ndikamoza kachitikengepu po go ndagota. Today its world language day. Proud to be mtonga mchanda

  1. ada bwana ndaonga, kumbi muja pani? so ise nase ndise watumbuka wa ku RU.Tikayowoya kuti boma ili lazula na wankhungu pela,wanyake wabisama kweni misana yili pamtunda yikuonekera!

 5. Chaponda the best way is to hang ur self man bcoz the hardness of the fire is growing bigger instead of ceasing ! If u r doing things in the darkness u must know that theres a light next to the darkness

 6. This is total madness, Straight out of black mirror, where were you all this time ACB and police officer? his office is already cleaned up and your busy fooling us.

 7. The maybe that there was government departments not utilized being an irregularity and corrupt intent of Chapobda.
  Reality it NO MONEY was lost or stolen because Zambia did not supply the contracted maize as requested in October and before the deadline in December.
  Any charges will be thrown own as no crime or theft took place possibly the allegations of conspiracy only,
  Nothing will happen.

 8. Amalawi ndife atulo amulekelela chapondayo tym yonseyo ask Dausi mesa amati choponda alive case period yonseyi sanawononge umboni? Ndife ogona amalawi tonse

 9. Which office? I thought his office was burnt? U waited this long so that his dirty plans to conceal the evidence shud come to pass & then u get to fool poor Malawians that this dunderhead is innocent upon the findings of ur search or enquiries. To hell with u all

 10. They Are Just Blindfolding Us They Know Each Other Nduna Ingamafufuzidwe Iri Pa Mpando ? Ndimaetsa Akanaichosa Kaye To Pave Way For Smooth Investigation THIS IS FAKE

 11. Vuto ndife obeledwafe ,tikulolera bwanji ndalama zathu kupita choncho osapangapo kanthu? wina akakubelan malaya pakaunjika wanu nde mpak kumuotcha.nanga uyu wakubelan ma million km muli phee .mphanv ndi anthu. wake up Malawians kukhala ngat mukulamulidwabe ndi azungu bwanji?

  1. Indeed we the Malawians We hv got aproblem. What is needed is inu muli ku ma Kolegi Try to force/assure the M R A to stop correct our taxes,because mbuzi zimezi zikamva kuti M R A yatolera k400,000,000,steeling will go highier,because they will know that M R A will collect another money. ANYONGENI OKUBA ONSEWO. ACB Mfufuzeni chaponda anagula farm ku mangochi Nakapa Vge, T/ A Bwananyambi. Ndipo Ana ena aku Chanco achitako ma practicals. Akulimako Chimanga ,Soya,ndi Mpendadzuwa. “KILL HIM”

 12. Hi professor, please just do one respected thing, lock up this guy his accusations are quite clear. Please do this for the sake of Malawians not for political interfearance, clean up your administration clean up corruption clean up Malawi have a good day.

 13. Amumange kumene galu ameneyu, coz mtundu wa amalawi ukuvutika ndi njra iye kungodya basi zindalama zambilimbili. Ndipo ngati pali ena awatchule nawonso akalowe

 14. analiko azawo amkaliseweretsa dziko la malawi coz amkazitenga ngati anazamanawo malamalo, samkadziwa kuti enaso anazamanawo kuposa iwowo, he could even tell the police to wait outside the gate till the time he wakes up. koma pano alikuti? the world is almost round

 15. Palibe chomwe angapedze ndiponso palibe chomwe chingachitike. Sitting minister moreover ndi senior komanso mkulu wa ACB anasankhidwa ndi president yemwenso sakufuna kumuchotsa Chapondayo mukuwona ngati angamupedze olakwa mwadaladala? Ndiye kutinso ngakhale mkulu wa ACB ntchito sakuyifuna. Akungokuphimbani kumaso chinyenga aphunzitsi kunamidzira ngati kuti akufufudza chonsecho palibe chomwe akuchita.

 16. That’s just for show to take us away from the truth that this puzzle will never get solved and chaponda along with all those accused will never be charged nevertheless jailed.that’s the Malawi l know

Comments are closed.