Malawi’s acoustic music icon Giddes Chalamanda has disclosed plans to go back to United States of America (USA) following invitation from fans.
Chalamanda said he is optimistic that he will travel to the USA for another music tour together with his wife Abiti Alafuledi.
In June, when he was leaving the country for USA, the 86 year-old musician said he was elated at the reality of travelling just like former President for Malawi Kamuzu Banda did.
The trip, dubbed the “Giddes Coming to America Tour” saw the acoustic musician together with other artists holding several concerts in Atlanta, Washington DC, and Indiana, among other places in America.
The veteran musician also attended workshops and held lectures on Malawian music and culture.
Chalamanda’s US trip was funded from money made through initiatives spearheaded by a group of Malawians that included artists Edgar ndi Davis, Macdonald Chapalapata, and lawyer Gift Mwakhwawa.
All the best oldman
Mphavu malume go konko
Wakalamba chonde uxapitenxo
GO back Giddy
Ukaneneletu kut malawi sadzathekaso
Have a #fantastic @journey my blue
Timaziwa kt ntchito ndiyophunzitsa anthu kotero koyenera kuti mukapeleke chiphuziso kuzera munyimbo zanu go well mr
zili bwino munthu wankulu, tikufunilanani ulendo opambana
God loves ugly is the song done by Me feat Jordin spark, I pity all local hiphop ,R&B artists of Malawi busy copying others talents, but you’re flops you can’t make it.you must embrace your culture first. Wishing you all the goodies Gides Chalamanda
Pitani basi mukasangarase anthu
agide tsopano mulungu ndi wadongosola agide anakakhala nyamata anakathyona koma zapeza atakula timakunyadirani kawonetseni luso la chimalawi chonde osawapondereza
Ney,considering his age,and the concubines he was hanging with the previous trip, that will be the end of him!
He should stay put, and enjoy his last years at home soil!
AZABWINO ZONSE
Anyamata a aneneli asatana akuchuluka kkkkkkk aneneli amilungu
zabwino zonse wakulu,mumatiimirira go go go.
Zabwino zonse
Sachedwa safulumila ndiye mulunguyo ameneyo
ulendo uno unditengeko gidde
Giddes ndi deal
Musapite ur 2 old maliro kudula
ndikudziwa kale kuti line mwana wanzelu ndiyo ikudya 1 kumeneko
Kkkkk simuri serious bro ndaseka kobasi
kkkkkkkkkkkkkk cctar monga inuyo simukudziwa ndikukhukupikila kuti imeneijayo ya line ija or timabebi ta chingro tikumafa nayo head heavy kkkkkk
Kkkk and kwa ine ndi nyimbo yokhayo ndimaiziwitsitsa ya amwene amenewa coz bambo anga ankakonda kuyimba akamagwira tintchito tinanditina pakhomo
inenso ndimene imandiwaza heavy poti pano ndunvela yomweyo kkkkk
Even at home we love him. God bless u madala
kd nyimbo mudaimba ija yoti” zikubwela mocedwa”mumaphelexela apa?God’s promises neva expire
A dream has come to pass, all the best.
Pitani baba
Asakhaletu atakayikisa software giddes
Zoona ogide kachikena loto lija litheka Lolita nda Abiti lija zonsezabwno wakulu
Bwana Thawe mukupezeka ukuku eti
Wamwayi ndi wamwayi basis zanu za yela baba ngakhale mukuoneka wachikulire Mulungu akapanga loan palibe oyisokoneza wish u all the best
umakwana gide!
Zonse Ndi Company Car
When Jesus Say Yes Nobody Can Say No!.. God Has Million Plans On Us Aswell But Its Matter Of Time We Dont Have To Rush Lets Wait Until God Fulfill Our Plans As He Did To Gides Chalamanda May God Guide Him Everywhere He Go…
Exactly thats true
God or Jesus??
Lucius! Do You Lead The Bible?.. If You Would’ave Know What Scripture Says, You Would’ave Also Know The Answer Of Your Question…
Bola osakajoyina #HOLLYWOOD,kkk!
Kkkkkk kukalamba ndkufu
Bola osakajoyina #HOLLYWOOD,kkk!
Akanapita ndi fans yavaya ku UN ija
Lol
Bwenzi akumawasangalatsa ndi live music ulendo uli mkati.
Pitani a Giddes. Bushiri anayamba choncho. Malawi wachuluka nsanje, mukabwera ndi Benz azati ndinu wasatanic. Bola mukapeza ka chiphaso ka maiko awiri (dual citizenship) kuti musamabvutike poyenda kkkkkkkk.
gidde ulibho
Wuuuuuu
congrants
Zikufika mochedwa zikutipeza titakula kale! kudandaula kwa Giddes chalamanda!
pitaninso bambo
Kkkkkkk axungu akufuna english yakeo
Go well father gidde
Wow! that so wonderful Giddes Chalamanda for lifting up our flag so high.
Bola akutumizileni return airticket man
waophula okulakula zikubwela mochedwa. zikutipeza titakula kale zikutipeza titakalamba……Gide umatiimilira. umakwana
I wonder what 50cent; Rihana; Doggy says upon seeing Chalamanda performing on stage }»
All de best mr giddes
Kuonetsa udolo pokanyanga nsambo, mpaka angelezi nkugoma ataimika mapilikaniro, apitenso basi, Mmalawi uyu apite basi , kuno kuno kuli madolo odziwa kutsina nsambo kuyambira uyu Gide, Danie Kachamba, Allan Namoko ,,,,, ,,,,,,,,,,,,,,,,,,