Residents living in villages of Nkhandwe, Thandaza and Kapanga in Traditional Authority Malengachanzi in Nkhotakota district are living in fear as a hyena appears during the night in these areas.
According to Samalani Saidi who is a resident of Nkhandwe village, people have now stopped doing things during night fearing the hyena that is threatening people.
“Whenever you want to walk at night you must be very careful since the hyena is also found the same time,” said Saidi.
Saidi proceeded by saying that in his village the hyena attempted to kill goats but people intervened quickly and rescued the goat.
People in the area suspects the hyena to be one of the wild animals that ran away from protected area of Nkhotakota Game Reserve.
Meanwhile, residents from the three villages are planning to report the issue to Nkhotakota Wildlife Office to intervene on the matter.
So far no one has been injured or killed by this hyena.
Anthu amaopa kusasaka fisi olusayo ,zina ndi za masenga
A game tithandizeni tisawaphe afisiwa amatiyitanila ndalama anthu amachoka kunja kuzawona afisi
Fisi ameneyu kangophedwa muwamva a mabungwe akuti mwaphwanya ufulu wa a fisi
Bwanji osadya inu amene mumamujambura
Akafika kwamakumba timuwaza
Kkkkk koma kwachema
Tiweja abwana akafika pa chia
mungoyankhula poti chili kwa anzanu si fisi m’modzi yenkha moti mpaka mmudZi mwa mgonba, malasa ndi ku bishop mtekateka adafika sikumudzi kokha ayi kma is not real hyena
Shania asamayendeyende mumu Star S Aims Phungu
hahaha nde mwati ndi kwa nkhandwe komwe? William Pastor Pota
People in Malawi fear hyenas, really?
Admin is selling Hyna at lower price ….
Koma Asalowe Mmujemwanganikuphananemnapondapataletuakulo
Shubah Abdul Karim Hk
Just kill it but bewere of reisen pple……….
Let the almighty God rescue people of nkhotakota from afisi olusawo
Kkkkk but did hyena is smiling
Someone is risen from the dead people. It’s not a real natural hyena.
Nanga wamgomba bwanji
Yoh!
Huhuhuwiiiiiiii kkkk koma na kwathu Ku Malawi iiiii
Alenje Alikuti tidye ndiwoyo.Paja Ife Nyama iliyose ndindiwo
Aaaa midzi yonseyo ikuopa fisi mmodzi bx muli azimayi okhaokha et
Man ,kuwopa fisi simantha, koma kuwopa ifa, ine nsadadyelele.
tikadakhala ife angoni tikadagwaza fisi ameneyo
kikiki
Watch out guy’s
Kkkk kaye chikayamba kulimidwa chidibwatu
hahahaha muzichita mantha ndinu,ife nkhani palibepo pamenepa
Kkkkk ku Sani uko kwao kwa afisi kkkk
Aaaah guys comeon. Fisi adakaopsabe? Chitnthu chamantha kuopedwa nd midzi ya anthu
so if this hyena appears at night where did u get the picture?? ma rubbish u 24
iweyo. nde idiot awa media reporter,amasungira zithuzi zosiyanasina
iwenso pa amako wamva
Ndinkhani yovuta kwambili ichi tchilombo sichimafunika kukhala pafupi ndi anthu chipedwe basi moyo ndiofunika kwawina aliyense posayang’ana kuti ndindani kaya wachokera kuti ai tiyeni tikondane a Malawi
Koma inu mukusewelesa ndiwo kà tango,bayani ndimikoñdo yobasi tikhwasuĺe ife iya mukamupha chonde ndiģawilenkoni ñdiimbileni phone pà # iyi 0631819701 am serious guyz
Iiiiii, mwachedwa nayo nkhaniyi, tinainva kale ma wk awili apitawo mokuti panonso anakambilana naye kale zinatha pano
Nanga ndi m’modzi kapena ambiri, naga ngati ndi modzi anthu amadera atchulidwawa sangaphe fisiyo? Mpaka kufika pachiwomphezedwe.
zakhala bwanji jamane, ndanesu wauka fisi
I loovee hyenas
am sure some1 is behind this ndipo ndakayikira PPD
Woo afisi aja ali pa #tour tsopano from Ntcheu to Nkhotakota afisi awanthu awa amavuta kupha
Kkkkkkk Eeeeeh mwanyanya kudya chamba!!!!
Ndie wokongolatu asaphedwe tizimuweta ameneyi wandisangalasa
Fisi ngati ameneyo adatulukanso mchaka cha 1988 chamu August to Nove amene adavulaza banja la bambo Sefa kusani ndie jamane zisadafike potelo pangilanitu njira yophera fisiyo
Ameneyu ndi wa munthu
Kkkkkkk madela ake amenewo? Aaaaaa Ndimunthu nzao ameneyo they must STOP kidding us!!
Ndubwera ndizamugwira ndine
ALI NDI MWAYI ANTHU AMENEWA NDIWO SIZIMAWASOWA AZINGOKHWASULA BAX
why nt ask help from our timasoja mu ma balakisi to hunt. and kill it b4 attack us ?
Knows How To Pause For A Good Shot! Photogenic Indeed – Goooood Appetite Too!!!
Shaaa my home
Kkkkkkkkk zinatheka bwanji mpaka fisi kujambulidwa bwanji kumupha nthawi yomweyo ngati anthu alipachiopsezo
samalani kumudzi uko anthu
Amangofuna chambacho osati anthu
Paja mdani wa fisi ndi msampha mungochera misampha pali ponse kumeneko
Kkk nde mwati mudzi wa Nkhandwenso ulinawo pachiopsedzochi?
Kkkkkk ukuona ngati nkhandwe siopa fisi eti kkkkkk
kkkkkjkkj
umaona ngt ndi mudzi wa mbuzi okha uli pa chiopsyezechi? kkkkk
mmmm
Hu uuuu!
Uyu sifisi ayi ndi gogo uja watisiya miyezi itatu yapitayo ndiye akudzawona zidzukulu zake musaopsyezedwe ayi ndi munthu ndithu ndikumudziwa eeeeeesh ndangodutsamo sindinatchole nkhwani . Muwafunse ayiniwake mudzi zambiri
eti bwànji muleka kumupha fisiyo pomwe mumamujambulapo kkkkkk
inu kodi ndnu mbuzi et? nanga fis akufuna chan malo a anthu. solve it!
Wina aphedala fisi wangayo…tionesanatu!
Fisi amayenda usiku kumene sim’madziwa??
Even wth bare hands i can kll a hyena
Am laughing at em haters like a hyena
Samalani akaka
Fisiyo ndiye tamuona koma nanga bwanji mumaleka kumupha pa nthawi yomwe mumamujambulapo?
Kkkkk analibe chida anali ndi camela yokha.
vuto ndiloti alenje aboma sangapite amfumu aletsa kuopa angakapeze minda yachamba
Afunse
kkkkkkkkk @ kungomuyang’ana basi eti
kkkkkkkkkkkk koma iwee kkkkkkkkkkk
Fisi wake ndi uyuyu? Eeeh ndiye ndi oopsatu
Kkkk
kkkk eee keep on aswana kwambiri anthu kumeneko kkk
Jamane afise asaphezeke ku mwala wa Jola ndiye akaphezeki kwa Nkhandi?
Imwi kaka a Mpenzeni musadandauli viwe alijufikaku kuneko akuru atheri cha mnemo mu nkhalangu ya Boma kaka
Zodabwitsaditu eti Mr Emmanuel Chimwaza
Akuchokera kuti jamane afisiwa? Muphiri la Sani? Afisi sakupezeka ku Mpamantha ndiye akapezeke uko, kakambani bwino jamane anya dada nda anya kaka
Inu ndaku town? Town yake iti mungatiuze inu mwene mwachoka kuti inu kuti mukafike Ku town mukunyadila inu man ganizani mofatsa musanapange chiganizo@ Dusty Chatepa
Aaaa hyena ndaphazinthu ine zoopysa..tanditumizilene transport pa airtel money ndikaphe kameneko
JOIN THE GREAT ILLUMINATI IN any where you are in the whole word today ; TO BE RICH AND FAMOUS whatsapp us on +23408130944146. Are you a man, woman, business man, student, military personnel, civil servant etc. that have longed wished to be rich and famous? Here is a great opportunity to join the world Great Illuminati Association. I promise you, if you are able to join your life will never ever remain the same, you will continue to experience breakthrough in the the works of your hand and you will continue to prosper. Please note that we don't share blood here and you must be someone that knows how to keep secret very well whatsapp us on +2348130944146
Come together and hunt until you kill it otherwise the hyena will eat your livestock
Kkkkk what happen again in my village !!!
Ndi fisi wamtundu wanji ameneyu?
Afisi a nthu
Bolani asamafike Ku Chididi ndithu
nanunso anthu akumudzi amachita mantha ndi fisi?
Eee apa ndiye zavuta osamayenda usiku
Kkkk musova achina kaka ndi dada.mungomuotcha muwazile dako.