Mwana wamwalira makolo ake atakana kuthamangira naye ku chipatala
Mwana wamwalira ku Zomba makolo ake atakana kumutengera ku chipatala kamba kazikhulupiliro za chipembedzo. Mwanayu, yemwe ndi wazaka zisanu zakubadwa, anadwala mutu ndipo m'malo mothamangira naye kuchipatala, makolo amwanayu anayamba kumupemphelera kuti achire koma mwatsoka,… ...