Mwina mwamwa kale ndiye tingoti pepani koma ngati simunamwe ndiye zachitika bwino.
Bungwe loyang’anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe lachenjeza anthu okhala mu mzindawu kuti madzi amene anatuluka nthawi ina mu madera ena mu mzindawo anali osakhala bwino.
Malinga ndi chikalata chimene atulutsa a bungweli ndipo ife a Malawi24 tachiona, pipe ya tudzi yolowera ku suweji ati inaphulika ndi kukhuthulila tudzi mu madzi amene akupita mu makomo a anthu ku Area 18A.
Aka ndi kachiwiri kuti madzi a mu mzindawu adzadzidwe ndi tudzi.
osadandawula guys ubwino wake mumazicha zilombo ndiye mukudandawula chani inube ndizilombo,kkkkk zimwani manyiwo basi kkkkk .
Timati tumbzi osati tudzi, Malawi 24 useless journalism
Mwatimwetsa mabibi a Chaponda inuuuu???
Mmmmmmmmmm! Gilberto De Sign
Mwamabe basi kjjkjjkkkj
kkkkkkkkk bola akuntsinje magaye kkkkkk
Kkkkkk amwa kale Prisca Manyozo Cecy Cee Makina Dennis Ben Chalema Glory Chihana kkkkkkkk
Kkkkkkk komatu iwe iwe
KKKKK munenepa manyowa kkk
Capital city yonse nkuzamwera pamenepaja, eish!!
ayimbidwe mlandu
Napepe
That’s weird how, how that possible?
Koma zoti madzi a mu Lilongwe amatuluka ndi tudzi zinayamba kumveka kale osati pano, apa zangophelezera poti zinaonjeza.
pepan nonse bolanso kumudzi.koma ndie munenep.
Gyz iiiiiii chocho
Uyu sanalembe bwino!
ii KOMA KHANI ZAKE MMMM,
Chifukwa chani pipe ya sewage imayenda pafupi ndi pipe ya madzi I only blaming Malawi Bureau of standards (MBS) coz if this were happening to sole proprietor company we were to hear that company “A” have been crossed due to none compliance very shame
same stories most of the tyms but nothing change….
Mmmm amalawi24 muziona zopanga post
It will take three months for the pipes to be clean…kkkkk mpedzedze ndi kuthulula mmiba is more likely to come.
Koma Guyz Amalawi24 amaganiza Bwanji? Ndadziwa mbuzi (amakonda kudya nyama ya mbuzi)
Kkkkkk ndiye mwat amwa manyi???
Madzi atudzi city. Kkkkkkkkkk two in 1 kudya ndikumwa at the same time.
PAYIPI ya THUDZI yaTHUDZUKILA eishh….sorry
This is ridiculous
kkkkkk tudzigate
Paja mumati nyau zimapaka manyi kukamwa ndiye apa azichepetsera ntchito gule alipo mwezi uno. Lilongwe water board yasintha dzina pano ndi Kang’wing’wi water board or Mbiya zodooka water board.
A water board apa anama. Zitheka bwanji pipe yamadzi mukalowe manyi? Apeleka madzi osasefa awa ndiye awonekela. Paja anthu akachedwetsa kulipira madzi mumawaduliratu ndiye pano mwawamwetsa manyi muwatani?
Aaaaa zowospa
Iiiiiiiiiiiiiii nyansi
koma guys a President ndi Vice president amakhala kulilongwekotu
Kkkk Tiye Nazoni A Biology, Mumanama Chichitike Mchana To the Water When Semeg Discharged In Water After Some Times. Gve 3 Postive & Negatve Of Sewege Discharge To The Organisims.
Amalawi zokangana izi kunene zoona kusowa zochitat uku basi kumalimbana eee mwamwabe kkkkk ai sitinamwe aaaaaaaaaaa
Inu mudzipeza ma headlines abwino ichi ndi chipongwe tu Kkkkkkkk
Mulemera anthu aku 18.How much in compesation pamenepa.
NO COMMENT APA NKHANI ZOPANDA NCHERE IZI.
Tudzi ndi deal
Disgusting
Oh!!!
waaaaa nono mukumwa madz amabi??baaaaaa nyama yose kununkha nsebwa zokhazokha
James Edward Mandambwe,
Shaaaaaaaa,.,…basi sindilipira madzi mwezi uno adzadule basi….iyaaaaaa
Aaashi! pepani kwambiri dziko mazi Ali tho mkumakamwetsa anthu mabi zoona Aaah! mwatikhumudwisa kwambiri simukuyeneranso kukhala fuko lathu inu tachokani APA Aah!
Mwangofuna kutchula tudzito
u fucked up… kodi uwona ngati lilongwe yense madzi angakhale affected osangonena area yake bwanj this is showin umbuli wako walembawe umafuna ma comments wagwa nayo apapa ur hate is more than ur vibe apapa ndee ndi zero pa ten
KKKKK koma ndatseka
Mind you, Ku lilongwe sikumakhala achewa okha.you know what,we’re always proud of our city and we’ll even die for it.
Ndye kudya azako pepani kwambiri
Mmmm komatu yo!
Manyi amakoma chonchi? Too good men
Kkkkkkkk musawawopo manyiwo azathu akulilongwe manyi sangaphe munthu chifukwa kukanakhala kufa titafa kalekale mmene tinali ana, chifukwa manyiwo tawadya mmene tinaliana sitinaFe bwanji
amwedwe matudziwo basi
titani poti tatani kale haaaaaa!
Ndiye wins adziti guys mubwere kuno, iyaaaa!!! Ndiye ndani adzalumwereni tudzito kkkkk musovenge
Hahaha koma presentation yake abale
bahahaha C’mon
Kkkkkkk tidzichewa tikumatuluka paka page aka ndi nyatwa.
tamangomwani iyaa mesa mumafuna zakudya za magulu? mu tudzi muli zakudya za magulu onse more over manyi ake ndi amabwana akuchokera mu zimbuzi zofrasha enanu sosage mwayilawira momwemo osangoyamika bwanj?
kona
Apa pali kumwaa manji ya mix navimavi kkkkk musovenge mwenkha uko muli warara akwaaaa
Muzikula,,osamangolengeza zilizonse
Mwamwa madzi otendela kkkkkkk
kkkk gyz mwasowa chonena bola ife tikumwa ndikunenepa kkkk kma
shaaaaaa
Paja ku Lilongwe ndi komwe kumakhala nduna zaboma komanso kuli State house? Yalakwa basi..
Kumwa ndi kumwa basi . Mumamwa zambiri kuposa zomwe mwawonazo .
Amweseni azinenepa
aaaaa yalakwa basiii
2bad
Zombwambwana.
Kulemba kwanji kwa nkhani uku.
Lllongwe ilekeni ife timaykondera manyiwo
Gule wamwa tudzi kkkkkk… Lilongwe town ya tudzi kkkkkkkk ndaseka kakakakkaak
kkkk madz amanyi hahahahahaha tandipaxen frozy ndisisire hahaha
thanzi mkudyayi dya zimachitika
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
koma olembayu akupangisa nkhaniyi kukhala yoseketsa heavy. akuti “yathudzukira”
thanzi mkudyayi dya zimachitika
Mwini mphale sada chara manyi anu omwe ameneo a Ku Lilongwe nu ife tili ko chipembe
hahahahahahhahahahaa! bola ine omwa a pamtchini
Hahahahahaha!! Kkkkkkiest CAPITAL CITY
Kkkk mchewa watokotatu apa!!!! Pepani aku Lilongwe
Shaaaaa
Kkkkkkkkk Koma Ndye2
Mmmmmmmm but kwathu kuno Mmmmm kusadwaradwaraku ndichisomo
Zikatha mbewa amanona ndi a…….. madzi abwino akasowa amapezeka ndi madzi akusuweji. Timwabee
Kkkkkk…… Koma fanz yaku Lilongwe amaionelera bwanj mpaka pamenepa…..aWater board mumuxiwe yesu ndi ophunzira ake
Ndiye kolera yalowa mu mabanja!
kkkkkkkkkk kaya muvuta kuti uthenga wabwela nchiyakhulo chanji, mwamwabe madzi a tudzi ..kkkkkkkkk
Malawi24 you are full of jokes , osalemba nkhani bwino bwino bwanj, nkhani ngat mukunena zamaboma
ayi abaleazanga womwe mwamwa manyi kungoti pepani
MAzi awulendo uno akukoma ndimadabwatu ine big up Lilongwe water board mubooleso paipi INA yatuvilo
Kkkkk za ulendo uno mukafunse nkasa zimene anapangidwa ndi chair
kkk matumbo anga kufuna kutuluka nkuseka kkki k isaaa!
Moyo waku Lolongwe okhalila kulimba mmm
Natural Recycle
kkkkkkk atolankhani enawa
…n’cifukwa mukutibulidwa
Kkkkkkkkk Koma water board yalero
Kkkk koma abale, kunenepa kulipo ndithu
No comment. ….
Kkkkkkkkkkk
Alwzy Lilongwe ndi more pazochita. Ine ndimadabwatu anzathu kusalara nkumati anzathuwa ndi Malawi wake yemweyu wa Chapondayu.
High grade of normal floras in there….kkkkkk….irony
Tamwakale komasikakomedwekake anthuni
Kkkkkk koma kumeneko!!!!!!!
kkkkkkkkkkkkkkk
mmene mwalembelamu padzadza kale fungo apa shaaaa!!!! mchifukwa chake tikunenepa mitu yokha ndi tuvi etiiiii????? madzi kumaveka ka acid,acid choncho mmmmmmh
so disgusting!! i will never kiss a chick from Lilongwe again
oh oh too bad
ahahaha koma aa,,,,,,, malawi24 sizathekaa,,,,,,,,, kupweteketsa ose okhala ku A18,,,,
Kikikikiki koma guys….
kkkkkkkk
Aliyes walemb apa manyi ali tho mimba mwake ndiy chachilendo ndi chan
Madzi asiya, ndengati awasiitsira dara
oh
Everybody deserve to drink that water coz its full of vitamins. Lol
You mean anthu amwa ndowe??
Omaigot
Nkulu udziyankhula bwino wamva? Talakwitsa kudzashopa ku capital?
akuluwatu aonjeza kkkkk
Ndikudabwa nawotu. Akufuna tichokeko kuno zolinga zathu zisanakwaniritsidwe?
Ukamati zavutanso ku Lilongwe China chomwe Chinavuta kapena chavuta ndi chani? What kind of journalism is this? ??
Waiwala 4months ago anathudzukilanso manyi mmadzi omwewo ku Lilongweko?
koma inu mesa soon mwamwanso madzi amanyi
Kkkkkkkkkkkkkkk…komatu zinazi muzitenge bwino eti…
ndi madzi osefukira osat zomwe mukunenazooo mudakhala bwanji a Malawi
Mpaka payipi ya tudzi, Malawi 24?????!?
Kkkkkkk kuthuzuka
Tamwa kale
Koma chichewa chakecho….
Hihi Ayiii
koma kuthudzuka mumakudziwa??
Tsoka ku lilongweko aaaaaaaa kaya
Wamwa kale? Takondwa Chakwawa
point of correction plz tayesesani kulemba muchichewa chachikhalidwe chabwino,if u elders u doin’ like this what about the youth,
Yathudzuka liti admin?
No wonder anthu a kulilongwe tikunenepa..team madzi a tudzi
khala serious
kiki
Tikudya bwino hehehe
Hahahaha
Sizowoona
Kkkkkkk koma abalee olembayu waganizapo bwanji? Ya thudzukira? Ngati tomatotu kunena kwake mmmm zovuta kobasi.
kkkkkk et et…….ndaseka heavy
aaa ubwino wake ndi apatalipatali
Kkkkkk Koma
kkkkkkkkkk koma lilongwe abale kkkkkkkk
Sory 4dat
nde matendatu amenewa
Kkkkkkkkkkkkkkk kumene
aaaaa apa tidwala basi
Chocho mkumati sumadya sete hahahahaha wamwa tubvi ta mnthalika uyoooo
Kkkkkkkk iwe suzatheka basi
chitosi cha munthu sichimapha ,, chinakakhala kuti chimapha bwezi chikutipha chikakhala mmimba mwathu
Mukaona nkhani zimenezi u post in chichewa cholinga kuwapanga provoke anthu kut atukwane kwambili. This is not good behave like u are professionals Malawi 24
Ambiri simumva chizungu kah kkkk
Kkkkkk Ishue Maulana
Kkkkk kma tisamatero
Paja tudzi ndichani!? Lol
Inunsotu mumationjeza kwabasi simungalembeko chichewa china
Ine kudabwa nsima ikuchedwa kupsa mwansanga monga mwa nthaw zonse hahaha ndie bwino ndibwele njodo
Kkkk madzi a nsimawo ali ndi zofunikira zonse kaya
Hahaha adha tidwala nazo njoka za m’mimbatu iz
Bansi akataika sawoleka amwedwa amenewo
kkkkkkkkk ooo yes
Nde mwati chathudzukila mmadzi akumwacho ndichani?
Paja Admn wa page imeneyi amakhala ku blantyre nanga kumeneku kunena kapena kugemula?
Timwabe
Ana atatu akomoka ndimimba kunyumba kwanga ndimadabwa kuti ndichani?? Agwidwa kolera akafa akandigulila amoyo ndithu
Choona nchopweteka koma chimamatsula,awuzeni chilungamo anthuo kuti amwa madzi oti muli manyi.
Kkkkkk true
tikati tudzi manyi ake siamakhala amasewela.ndiaja wekha kunyela mkumadabwa kut waonjezelapo ndani.kikikik
Kkkkkk Koma You .#Moses usandikomokese ine
Kkkkkkk
Kkkkkkk
Ikakhala nkhani ina mumalemba mu English nde tinene kuti iyi yaphweka polemba mchichewa? kkkkk @ Malawi24
amweseni amazitama kt ndi zilombo achewawo. hahahaha akavale zigoba
Stupidity at its epitome. Does lilongwe or central region habour chewas only?
uyu galu weni weni kuzolowere kukulira ku minda ya tea etii? zukhudzana bwanji ndi achewa apa?? unava kuti ku lilongwe kumakhala achewa okha?? mbuzi iweti,kupusaa! ngati ulibe choyankhula osangokhala chete bwanji??
zikugwilizana chani ndi mtundu wa munthu. thats y sitikutukuka amalawi(mindset change needed)
Ndiwe Wautsilu Lilongwe Sikuli Achewa Okha,
marijuana is not gud for your chicken sized brain.
Abdulz Duwez Adamz this this crazy comment kkkk
Koma iwee mmmmmmm
Iwe ulibe nzeru eti mutu mwako muli ma tudzi okha okha eti ? Ndiye kuti siwuziwa kusiyanitsa pakati pa zilombo ndi achewa . kuyambila lero udziwe kuti gule ulingati mpingo amati mpingo wa aloni ndiye ngati umapita ku tchalitchi siwe wagule ndiye usamawone ngati achewa ose ndinyawu wamva?
haha koma adha awa andiseketsa???
tikamati ku Malawi anthu ambiri ndi osazindikira wina ndiameneyu. tikamati dera lili ndimbuli kwambiri ndi kummwera kuno..chitsanzo chake ndichimenechi. kusayendatu uku.
Siachewa onse amene amapanga zanyau u have to listen to ur mind before commenting this dude
mumwabe mabiwo basi abwanyanga inu. ngt ili ngoz bwanj sichitika ku blantyre kuno hahahahahaha mukhaula
Hahahahahaha kodi ndiye kut ndi zoona?
Kkkkkkkkkk kod chilombo chimamwa mazi abibi kkkkk
kkkkkkk koma ku Lilongwenso nde ayitu
Lilongwe yose njanyawu tereku gule kwao
Kkkkkkkkk so fucken badminded
kkkkk koma ndaseka
Brother achezeni bwino azanuwaaaaaa
tikhaulitsana povota.ndi minus pamenepa.
Kkkkk mavuto oposa size ya2
mmmh ife tingot sory
mmmh ife tingot sory
At least mukanalemba kut payipi yanthudzi bwezi tikuganiza zapansi pamtengo wakachere
tudzi ndi chan? meaning
DirtYswAG
Lero limenelo mukudana nawo manyiwo Admin? Nthawi yomwe munali kakhanda simwadyayidyapo inu.
ubwino wake Peter amakhala ku Lilongwe tamwa tonse bansi
Koma atolankhani awa amawatenga kuti?
Kkkkkk koma Chichewa chinachi abaleee, YATHUDZUKILA??? nde kt chani?????
http://Www.malawi-water @tudzi.com . SHAME.
Manyiso mkachani? Ndimaona ngati udziti Acid kapena ndulu ya Ng’ona.
koma abale imu
kkkk
Tumwe tumwe
kkķkkkkkk chonenepetsa nkhumba sichiziwika asiyeni amwe zimenezo
Mukafa Tikakuikani
What kind of reporting is this? Kkkkkk
kkkkkkkkkk eeeeeee npaka tudzi man
kkkkkkkkkkkkkkkkk koma
koma olemba akewo
ok
Koma madzi agulitsidwadi?
Kkkkkkkkkk sindimwaso
Iiiiiii hahahaaaa Malawi! Malawi! ….kkkkk timwerere
Ndimadabwatu kuti nthawi yozizira sindinkamwa madzi, koma mmene ndikumwera pano, nde akukoma bwanji, angophulitsiramo ma pipe onse ndi2
Kkkkk
Kkkkkk kumalawi muli pa mavuto eish
kkkkk akanadandaula akanati muthu umafa akamwa madzi atuziwo koma safansoyi,akangosanza basi
Mmmm.Sndmwa madz loxe lalero.
mudzafa yifa yowawa
Ine Ndimadabwa2 Kuti Madziwa Kukomaku Bwanji?
Oh my God!!
Kkk
Koma nkhani zinazi tamalembaniko mzilankhulo zina ngati #Chiyao kuti enafe tisamamve nawo za nyasi ngati zimenezi #NdasanzaEishhhhjhhhhhh
Kkkkk timwee basi muli thanzi mmenemoo
Kkkkkkkk mwamwa kale kkk
kkkkk basi amwawo mene awerengamu akhozano kumakasaza
Xkkkkkkk mtolankhani iwe kumazimitsira ngati chilli cha nkhotakota
ok ?
Koma ku lilongwe abale kulilongwe
tamwa kale ife kkkkkkk
oh oh
koma zowopysa mesa miyezi yapitayo manyi analiso khathikhathi m’madzi akumwa ku Lilongwe konko, koma kumpanje eish! !!
kkkkkkkkk amwelere basi
bola tadziwa inu muli ku? abale anu ali ku?
Kkkkkk kulemba kwinaku aaa kwiii
Fuck u
Mmm inu tàzisiyeni zimenezo tudzi tikaipe pano poti mwakula?mwaiwala a adimin munkamwa madzi a tuďzi mukabibidwa iñuu!!!
Wawa!wawa!!wawa!!
kkkkkkkkkkkkk muuzei adminiyu mwina wayiwala
Hahahahahaha koma anthu muzikhala serious
Ndekut nawe wamwa michimba et ???
Hehehehehe uko uko nde mwati adim akulira madzi amanyi
kikikiki admin mawa imwa madzi amanyi koma pipo
Shaaa
Aklankhula bwanji ngati sanavekedwepo matewera
Pepani
ku malawi!!!kodi chimakhala chili chani?? ufiti, mkhaza, kaduka??
ndamwa kale2.
kkkkkkkkkkkkk a tokankhani npake ayamba kukwapulidwa makofu,mumalemba udyooo
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk