Zavutanso ku Lilongwe: payipi ya tudzi yathudzukila mu madzi akumwa

Lilongwe Water Board

Mwina mwamwa kale ndiye tingoti pepani koma ngati simunamwe ndiye zachitika bwino.

Lilongwe Water Board
Tudzi mu madzi akumwa

Bungwe loyang’anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe lachenjeza anthu okhala mu mzindawu kuti madzi amene anatuluka nthawi ina mu madera ena mu mzindawo anali osakhala bwino.

Malinga ndi chikalata chimene atulutsa a bungweli ndipo ife a Malawi24 tachiona, pipe ya tudzi yolowera ku suweji ati inaphulika ndi kukhuthulila tudzi mu madzi amene akupita mu makomo a anthu ku Area 18A.

Aka ndi kachiwiri kuti madzi a mu mzindawu adzadzidwe ndi tudzi.

Advertisement

260 Comments

 1. Chifukwa chani pipe ya sewage imayenda pafupi ndi pipe ya madzi I only blaming Malawi Bureau of standards (MBS) coz if this were happening to sole proprietor company we were to hear that company “A” have been crossed due to none compliance very shame

 2. It will take three months for the pipes to be clean…kkkkk mpedzedze ndi kuthulula mmiba is more likely to come.

 3. Paja mumati nyau zimapaka manyi kukamwa ndiye apa azichepetsera ntchito gule alipo mwezi uno. Lilongwe water board yasintha dzina pano ndi Kang’wing’wi water board or Mbiya zodooka water board.

 4. A water board apa anama. Zitheka bwanji pipe yamadzi mukalowe manyi? Apeleka madzi osasefa awa ndiye awonekela. Paja anthu akachedwetsa kulipira madzi mumawaduliratu ndiye pano mwawamwetsa manyi muwatani?

 5. Kkkk Tiye Nazoni A Biology, Mumanama Chichitike Mchana To the Water When Semeg Discharged In Water After Some Times. Gve 3 Postive & Negatve Of Sewege Discharge To The Organisims.

 6. Aaashi! pepani kwambiri dziko mazi Ali tho mkumakamwetsa anthu mabi zoona Aaah! mwatikhumudwisa kwambiri simukuyeneranso kukhala fuko lathu inu tachokani APA Aah!

 7. u fucked up… kodi uwona ngati lilongwe yense madzi angakhale affected osangonena area yake bwanj this is showin umbuli wako walembawe umafuna ma comments wagwa nayo apapa ur hate is more than ur vibe apapa ndee ndi zero pa ten

 8. Kkkkkkkk musawawopo manyiwo azathu akulilongwe manyi sangaphe munthu chifukwa kukanakhala kufa titafa kalekale mmene tinali ana, chifukwa manyiwo tawadya mmene tinaliana sitinaFe bwanji

 9. tamangomwani iyaa mesa mumafuna zakudya za magulu? mu tudzi muli zakudya za magulu onse more over manyi ake ndi amabwana akuchokera mu zimbuzi zofrasha enanu sosage mwayilawira momwemo osangoyamika bwanj?

 10. Kkkkkk…… Koma fanz yaku Lilongwe amaionelera bwanj mpaka pamenepa…..aWater board mumuxiwe yesu ndi ophunzira ake

 11. mmene mwalembelamu padzadza kale fungo apa shaaaa!!!! mchifukwa chake tikunenepa mitu yokha ndi tuvi etiiiii????? madzi kumaveka ka acid,acid choncho mmmmmmh

 12. Ukamati zavutanso ku Lilongwe China chomwe Chinavuta kapena chavuta ndi chani? What kind of journalism is this? ??

 13. Mukaona nkhani zimenezi u post in chichewa cholinga kuwapanga provoke anthu kut atukwane kwambili. This is not good behave like u are professionals Malawi 24

  1. uyu galu weni weni kuzolowere kukulira ku minda ya tea etii? zukhudzana bwanji ndi achewa apa?? unava kuti ku lilongwe kumakhala achewa okha?? mbuzi iweti,kupusaa! ngati ulibe choyankhula osangokhala chete bwanji??

  2. Iwe ulibe nzeru eti mutu mwako muli ma tudzi okha okha eti ? Ndiye kuti siwuziwa kusiyanitsa pakati pa zilombo ndi achewa . kuyambila lero udziwe kuti gule ulingati mpingo amati mpingo wa aloni ndiye ngati umapita ku tchalitchi siwe wagule ndiye usamawone ngati achewa ose ndinyawu wamva?

  3. tikamati ku Malawi anthu ambiri ndi osazindikira wina ndiameneyu. tikamati dera lili ndimbuli kwambiri ndi kummwera kuno..chitsanzo chake ndichimenechi. kusayendatu uku.

 14. koma zowopysa mesa miyezi yapitayo manyi analiso khathikhathi m’madzi akumwa ku Lilongwe konko, koma kumpanje eish! !!

Comments are closed.