Tikunyenyaninyenyaninso 2019 – Mutharika auza a Kongeresi: ati a Chakwera apinyolitsa chipani ngati Yudasi

Advertisement
Peter Mutharika

Ndi kutheka onyoza amawanena a Chakwera kuti ndi Yona othawa ulaliki koma mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika ati a Chakwera ndi Yudasi basi okonda ndalama.

A Mutharika dzulo ananyogodola a Chakwera kuti apinyolitsa chipani cha Kongeresi kwa a Sidik Mia. Ati pa mtengo wa K200 miliyoni.

Peter Mutharika
Chakwera: Anenedwa kuti ndi okonda ndalama

“Pofika 2019, patsala DPP yokha basi,” anatelo a Mutharika pa msonkhano omwe anachititsa pa Biwi mu mzinda wa Lilongwe.

“PP ndi ija mwini wake anathawa ija, ikakhala Kongeresi ayigulitsa dzana lomweli ili ku Chikhwawa kwa mkulu wina wa malonda,” anatero a Mutharika uku owatsatila akuomba m’manja.

Ngakhale sanatchule a Mia, a Mutharika amaoneka kuti akunena kuti Kongeresi yagulidwa ndi a Mia amene alowa chipanichi loweruka kwa Ngabu.

“Ikafika 2019, tikunyenyaninyenyaninso,” anatelo mozitamandila a Mutharika.

Dzulo kanali koyamba kuti a Mutharika athililepo ndemanga pa kupita kwa a Mia ku chipani chotsutsa.

Pa msonkhano omwewo a Mutharika adanenetsa kuti Boma lawo lipita chitsogolo ndi ndondomeko yopatutsa madzi mu nyanja ya Malawi kuti azipita ku Lilongwe.

Ndondomeko imeneyi yakhala ikukaikilidwa ndi a mabungwe komanso anthu ena ati kamba ikuoneka ya katangale.

Advertisement

443 Comments

 1. Tikamawerenga Buku Lomwe Agwitsa ntchitolo, Timamva kuti Davite Mwa Wa Banja la jese Anasankhidwa Kukhala Mfumu Munthu amene Anali koweta Nkhosa,mzotheka Achakwera 2019.

 2. mukazaona munthu akukamba zaneba wake ingoziwani kt amamuopa kwambiri,,,afro barometre unapangilanji zimenezi ona nkhalamba zikusowa mtendere pano

 3. Koma anthu ena, mukunamizana kuti yona alimba, ali m’mimba yansombatu akukamutayila ku chuch kwake, ndichifukwa mcp muli mabvuto adzaoneni chifukwa mtsogoleli kulibe anamezedwa ndi chinsomba, zandale sazitha kwatsala kuti akafika ku nenevi akapepese mudzaona pofika 2019

 4. God is not Mutharika nor DPP, come 2019 only God knows. Those who are pro dpp are devils agents, corrupt figures, evil cannisters. A normal thinking and God fearing human being cannot go for dpp. Zachulukaso paforum iyi kukhalira kumbuyo dpp ndi mbuli, a gong’oli and boot leakers, useless cowards who cannot talk sense

 5. Dpp could win if msowoya joins them.The coming of mia means alot to the political landscape of the country.Peter will get msowoya then North malawi will b blue kkkkkkk

 6. Koma Inu Achakwera Ndiye Boma 2o19 Mwaiwalanso Banja Lonyonzana Limakhala Nthawi Yayitali Dpp Yatithopetsa Ndikhalidwe Lake, Education , For Secondary Xool Mkuganiza Kuti Mwana Kuchokera Form 1 Up To Form4 To Write Maneb.

 7. Mcp Samala Ife A Dpp Ndilipo Ndipo Ma Cardet Ena Mwiwo Ndife Tikuswan 2019 Tinatopa Ife Ndiulamulilo Wanu Mumatiika Mu Drum Ya Chitez+gonji+phulusa Nkhani Yake Yongotchula Bakha Wanu Uja Kamuzu Iyaaa Ufulu Kwaufulu Pano Iyaaaa

 8. People Should Have To This:
  The National Registration That You Are Doing Is What It Gives More Powers To The Dpp Members.
  Anthu They Never Know Kuti Kalembera Yemwe Mukuchitayo You Are Voting That Time There4 Palibe Chowalepheretsa Awa Akubawa(dpp Theafs/robbers)kumayankhula Molimba Mtima Like That Saying #coming 2019 Mcp Inyenyedwanso.Enanso Ma Page Ngati Awawa Malawi24 They’re Involved In That Foolish Encouragement Kwa Anthu Instead Of Talking About Crisis Ya Frames Mwina Ambiri They Can Take Reaction On That.

 9. #Synet ukafunse Zuma ampangila zionetselo katatu kuti atule udindo amulephela mpando waprezident Chakwela ndi Yonadi 2019 DPP ndi Boma basi kumalawiko sindikuona chipani chomwe chikhoza kupikisana ndi DPP

 10. AAAAA! kaya koma tikungotaya nthawi ndi kumanyozana tokha-tokha anzathuwa ndiolemela kale.Tikati tiwone pa mitu yakayendesedwe kaboma achakwera nawonso alikale m,boma pano.

 11. Kodi kachimutuyu alive manyazi folena uyu kakaka ukazaluza uzathawa iwe hehehe sindinaone munthu wamkulu buzy ndi ana osamayankhula zachitukuko bwanji buzy kunyoza tikayamba kubweza moto muli tikunyoza boma zachamba bax simutitha apa

 12. Bwana sionse omwe akukondwela ndi ulamulilo wanu ngati mwatopa asiyileni azanu coz cholinga cha inu mukufuna mungoona dziko la malawi basi

 13. Nonse Ndinu Makanda Pandale,munena Zaena mupange zanu,mukunyoza mtunda wina,madolo anuwo 2014 anali kut?kuyendesa,nkhonde,mtumbuka,mshona,yao,mchewa,ngoni,mang’anja,bathwa,nsena,musayese chophweka,mukapambana nanuso muzadedwa aliyense afuna tribe yawo ilamulire zomwe ndi null set,dziko si mbumba yakwanu muzingolima fodyayo nchikulire

 14. Its rediculous to tell people that u will win the election despite all blunders u r making while u r in the same government.Mr President u r a professor through education but look at what is happenin in education sector.For instance how on earth can a primary school teacher stay at college for five yrs in the name of producing quality teachers?a secondary student sitting for examz after 3yrs are you expecting that kid to pass it?This current syllabus is full of challenges.Malawians have eyes and ears.

 15. vto ndlakt amalawi tmakhulupirir kt munthu akaphuzra kwmbir bdy ali nd zeru zautsogoleri.Ati anal kw america tmuvotere mchfkw chke adabwer kzaba basi.Amalwi munth akphuzr ndalam zmwe amalandl patchto ymwe akgwr zmakhl zake osat zadzko ndy pot peter anaphuzr mmaona ngt ndalam zake azayndetser dzko kkkk.wethr u lyk it or not bt chakwera is leading this country in from 2019 aft elections.

 16. Vaccancy announcement tenable at state house,vacant post HEAD OF STATE (PRESIDENT)anyone can apply male or female of malawi origin closing date of receiving applications is 19 may 2o19, method of application by hand to your nearest district comissioner .

 17. Malawi wadzudzika nikale chonde Ambuye tichotsereni mnthuyu asadzawinenso chonde Ambuye Mulungu pitala Bwampini Chikutumbwe Matchona nzika yakunjayi ngakhale mwana wake sakudziwa dziko lawo achoke mnthuyu 2019

 18. Khalidwe laanthu ochimwa ndikunyoza azawo basi,komanso munthu amene alibe cholowa ndizinthu za mulungu nthawi zonse amangodziwona iye okhonza pamene anthu ena onse amakhala olakwa.ntchito kuloza anzao olakwa tsiku lina mudzaona kuti Mulungu samapangana ndi munthu poika munthu pampando.inu amene mudawina sinzeru zanu koma kuti Mulungu adalola kuti mutsogolele mwanthawi yanu,chinamuvute ndichani kukuchotsani ndikuika munthu amene simukumuyembekezera,popeza mau amati Mulungu amapha komanso kupereka moyo,iye amatsitsa ndikukweza munthu pampando!1samuel 2:6.

 19. 1994
  1:UDF
  2:MCP

  1999
  1:UDF
  2:MCP

  2004
  1:UDF
  2:MCP (Mosogozedwa Malemu Bingu Muthalika ndye Chfkwa Chot #BAKILI_MULUZ Amkachuluka Mzeru Nd Anamuthamangitsa Ndpo Nthawi Yomwe #MUNTHALIKA Anayambitsa Chipani Cha #DPP

  2009
  1:DPP
  2:MCP

  2014
  1:DPP
  2:MCP

  Inu A MCP Muzngonyadra Kamba Kot Mumakhala Pa #Number2 Pa Chisankho Chnachilichonse…

  #DPP_2019_BOMAAAAAAAAAA!!!!!!!!!!!!!!!!!

 20. The truth is being told in our own eyes, the Ngabu rally has shaken them up!! The table turns , lets wait n see. Cant fool them all the time remember.They are looking for change .

 21. Kkkkkkkkkk tamusiyani Petulo uyu mutu wake sukugwira chifukwa wakhala akamunyengerera Sidiki koma adamukana kwamtuwagalu kuwonjezera apo ati kusankha Atupele kukhala nduna yaza health chosecho sanaphuzireko college yokhudzana ndi health,ndithu wasokonekera apite ku Zomba akachire kuja kwa amisalah

 22. Ukat ndikunyenyani iwe ukuona ngat azakupase mavote ndindan? Tapanga zimenezo uone. Yemwe ukufuna umunyenye lero mmawa ndiyemwe adzatsitse makatan mnyumba mwako, adzatulutse mpando, adzakoleze moto panja panyumba yako iwe utatsinzina. Teyenazo!

 23. Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana

 24. Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana

 25. Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana

 26. Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana

 27. Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana

 28. Ndi nkhosa yotayika ija ibwezeleni ku khola paja ikasowa zizake imakhala kuti yayamba misala mkhululukileni nkuluy nd misala ndthu agwade pasi asale kudya ziwanda zichoke DPP woyeeeeeee!!

 29. You are just talking as children bros and sistaz.Can mcp make it, realy? with tambala wakuda and kwacha slogan? am afraid.Is Mia more powerful than Chakuamba who failed to kwachalise southern region? Let us give professional political statistics to the masses.

 30. Guyz mantha ayambila patali munthu akakhwima nzeru zimachepa apa DPP idakalamba 77years mtsogoleli atsogolela bwanj? vote yanga ngat akuifuna andipatse 88800000 chifukwa wakalamba uyu.

 31. Nanga Apulesidenti akunama kuti othawa ulaliki?,kodi mungakhulupilire bwanji munthu osiya zaCHAUTA kuyamba za ndale kuti angakhaledi mtsogoleri wabwino?.Ziwani izi:maonekedwe anthu ndiomwe amaonetsa makhalidwe komanso makhalidwe athu ndiomwe amaonetsa tsogolo lathu.

  1. Religion & Politics R The 2 Sides Of The Same Coin.U May Wish 2 Ask Why?Coz Pple Who save God In Different Religions Are The Same Pple Who Found, Form,join,participate In Different Political Parties Depending On Difrent Degrees Of Doing Things.

 32. Nkhalamba Yawoyo Sitidzayivotelanso Ife, Siyiyankhulanso Zomveka Kukhala Mkamwa Muli Miyala………2019 Ulendo Wakumudzi Kwawo Ameneyo

 33. Chakwera ndiudasi mpata alibe ameneyu mulungu amulange.go back were you were that’s it to you Dr chakwera

 34. m.c.p 2019.boma amalawi muzakhala chocho mpaka liti anthu ozaganiza inu mumakhala ngati munabadwa ka mbuzi bwanji mwanyela pososa aDPP .muonaso mwanya nazoni ..just look another countrys in Africa alipheee kandalama kao kamphanvu osati panyasaland mmmmmm.munabadwa ku anthu or bwanji ..aaaaaaa oho nazoni .2019MCP bomaaaaaa

 35. MCP moto kuti buuuuuuuuuuu,wina alira,Lucius chokangoyimba pa nsonkhano wa MCP anthu m’mimba kutsekuka kuyesa kuti mwana wa dziko walowa chipani choyenera, lets wait and see 2019

 36. Kusonyeza kuti iyeyu akuziika mgulu lowina? Kkkkkkkkkk moti sakuona komwe ma voti akupita ndiye kuti? Bp ikaza shooter tizakaika kundata farm osadanda mwene

 37. Kicks of adying horse. Instead of minding your own business of hw you cn transform yr corrupt party, you’re busy talking abt chakwera. Hmmmm!!!! Inu mwagwa kale, jst wait and see!!!!!

  1. This is his business my brother and that’s what politics is all about, do you expect him to applause the opposition? The fact is, it’s none of your business neither mine. Let them insult each other!!!!!!

 38. Kuchita Matha Kumeneku, Wayamba Kuyataya Mtsogoleli Pagulu Ngat Apa, Liliratuni A Dpp Boma Lakukanikani Ife Mcp Boma Wina Ufune, Usafune Unyenyedwa Ndiwe Wa Dpp .2019 Subelanso , Mcp Moto Kut Buuuuu !!!, Voicing Out Views Freedom Of Expressions.

 39. Awatu kunyenya amakudziwa osaiwala pajaso Bingu anadzinyenya ekha kkkkkkk ife tilipheeee kudikira 2019.DPP chipani chobela a Malawi

 40. palibe muzanyenya ndani muzanyenyeka nokha mukutenga ziko ngati lambuyanu .kusogolo kuno azatha anthu nmalawi kumangopita kwa eni ..2019 alukamwaso phala pitara .kkkkkkll

 41. Shuwaditu Bwana Peter tinyenya nyenya ife tambala wa black Lazarus wawuphawi abwelele ku nyumba ya Mulungu, kulira ndikosayamba ku MCP atibela atibela mudzingolira ndipo mudzaliranso 2019.

 42. Hahaha ngakhale ndabwera mochedwa , ngati simukuopa chakwera bwanji mwayamba kale campaign? Ino sinthawi ya campaign, khala pansi nkhalamba iwe wachabechabe..tidzavota ndife anthu osati iweyo..M.C.P ndi boma Kale win afune or asafune.

 43. DPP will die come 2019 believe me or not. I was a strong member of DPP but with what it has done it has disgraced me.Education yawonongekelatu boladi a Chair analinso bho

 44. Kodi mukanena kuti boma silimaluza amavota ndi anthu okha omwe ali bomamo mesaso akunja kwa boma nafenso timavota ku Zambia bwanji chipani chosusa boma chinapambana tatopa ife ndi ulamuliro wa dpp tikufuna tione dzina ife 2019 dpp yikugwa chagada basi!!!!

  1. ngati ndinumulungu mwawina koma ngatindinumunthu basi mudikile kumbukirani mumene tinadandawulira ndi bingu ndiye alikuti choti muziwemulungu si james ndimulungu basi.

 45. ndizona kt yudasi anagulisa yesu ndipo akhristu osatila yesu adataya chiembekezo kt kwatha koma patangopita nyengo zipaso zochokela mkugulidwa kwayesu lunayamba kuoneka ndife pano lero tikudyerela ufulu kuchokela pakugulisidwa kwa yesu…….so ngat mcp yagulisidwa ndekut tasala pang’ono kudyerela ufulu wakukhala mmalawi onse osowa nthito ibiliv in the name of God through chekwela tizapeza nchito…….aphunzisi azayambaso kumva kukoma pogwila ntchito zao……..amen

 46. ndizona kt yudasi anagulisa yesu ndipo akhristu osatila yesu adataya chiembekezo kt kwatha koma patangopita nyengo zipaso zochokela mkugulidwa kwayesu lunayamba kuoneka ndife pano lero tikudyerela ufulu kuchokela pakugulisidwa kwa yesu…….so ngat mcp yagulisidwa ndekut tasala pang’ono kudyerela ufulu wakukhala mmalawi onse osowa nthito ibiliv in the name of God through chekwela tizapeza nchito…….aphunzisi azayambaso kumva kukoma pogwila ntchito zao……..amen

  1. When did a teacher enjoyed his work in malawi? Ask those who are still around and were teachers during mcp era, I have one as uncle here, he will opennly tell you kuti during mcp uphunzitsi was complete slavery, not only it, police, nurses, prison officers etc were receiving peanuts bolako pano they can fight for their rights in as far as renumeration is concerned but during mcp umatengedwa ngati oukila. Apolisi kukakamizidwa kuvala makabudula ati uniform. It seems you do not know what you are saying by insinenuating that aphunzitsi azasangalala ngati kale yet were sleeping on empty stomach, mbuzi iwe.

 47. Amuthaka mukamati achakwela añasiya kusogolele ñkhosa zamulungu iñu mukusogolela agalu amuluñgu?.tazilañkhulañi bwiño

 48. Zotsatila zamavoti pa fb ndi MCP 60% DPP 30% anthu ammizinso I hope azavota pa fb pomwepa alinso ndi ma Android phones I gues kkkkkkk

 49. Amuthalika akuopanji, why targeting MCP each n every tm? musiye chakwera adzawina ndi2 or umudetserere.

 50. ndiye kut atupele wagulisa chipani 4 dat matter ndi president wa udf akutani ku dpp ndipo mia sanali president kambani zina

 51. Kulowa kwa Mia Ku MCP it’s normal koma akangowasakha kuti adzakhale running mate that’s destruction. Msowoya ndi amene ali bwino kunena zoona comparing to Mia.

  1. I agree with, Msowoya can be good for Vice president administratively than Mia. But Mia is good politically; he has far much votes than Msowoya. Msowoya adavutika kuwina ngakhale dera la kwawo

 52. Tieni Tizingo Kudyasima Ndikukhuta Bola Chakudya Chizipezeka Coz M’tsogoleli Mwini Wake Yehova Akumudziwa Tsono Tieni Tikondane Pamenepa Ndioneke Mbuli

 53. I wonder anthu kumanena kuti chakwera wathawa ntchito ya mulungu kusankha u president, are you telling me kuti utsogoleri wa dziko ndiwa satana?bwanji inu nomwe mumanena kuti utsogoleri amapereka ndi mulungu?its possible mulungu yemweyo akufuna kukonza zinthu.

 54. Good day my friends I am so happy to share my great testimony to my friends on Facebook and Twitter all over the world I was a HIV patients for 6 year my friend introduce me to DR ABUMEN who cure me from the deadly virus I am now negative now I am a living testimony if you are affected with this virus because when u keep silent the virus will eat you up, You can also email him for any kind of help via email ([email protected]) or whatsapp him on +2347085071418.

 55. Dpp Mafuta Atha Mu Tank Ndiye Ikuenda Koma Mokakamiza Pokana Ukhumudwitsa Oitsatira 2019 Ifika Koma Movutikira Ndipo Ulendo Uluthera Pomwep

  1. Or zauzika ndaDInditsaso madoro nde mudzit sindr ku malawi kuno koma chakwera zot nkulamulra dziko kkk ay ndithu ngat ul ndi nkungu kavote koma yanga sindingabetse chifukwa udas ngat amene uja.

 56. Ine sindiyankhulapo kanthu kuwopa ma member anzanga a mcp.Komabe tiyeni tivomeleze munthu(peter)abusa athu aja sangamukwanise.

 57. Are you looking for a way to get rid of hiv/aids and everything seems not to be working, you have been criticized because you are positive or you can’t live to the fullest because of your status, sometimes your happiness turns into sadness when you remember that you are positive and you start thinking what will happen to your children or family, my brothers and sisters cry no more and be sad no more God is not asleep there are no problems without a solution, Dr Abuu made me believe that all problems has a solution contact Dr Abuu anytime anyday for your HIV problem to be over, he has cured a lot of people and i was cured too by his medicine, please beware of those people claiming they were cured by some doctors i have lost money through them until God showed me the light by meeting Dr Abuu, i can’t keep this to myself i have to share to save lives just as mine was saved, whatsapp or call his number +2348066454364 or send him a message on his email address [[email protected]] contact him and thank me later God bless you all.

  1. Muchedwa nazo boma timasitha pakatha 10 years basi don’t waste your time aa inu ndi munthu wabwino wanzeru I know u bwana wanga

 58. Koma Nkhalamba Iwe Ukuganiza Kuti Timakukonda?Shame On You Mr Mugabe.2019 Is Not Yours,77yrs Koma Kuganiza Ngati Mwana.Za Mcp Zukukhudzani Bwanji?Mthira Kuwiri Iwe

 59. Guyz guyz , Ndikurangizeni Azanga nonse otsatira za Dziko anthu awa ndima Guy zawo ndizimozi sayambana ayi amagwirizanaso zed koma amafuna azipusisa opusa ndiye tikumayambana ndife amphawi iwowo mkumaseka Ali phee akudya ma supergt pizza ndi pk akakakumana Dziko la azathu lija ngat Ku RSA. aa KFC sinkhani ife kuno titadurirana malire kutemana, kuphana kumene wawa ati wina wanyoza Pitala sunamuone sukuziwa

 60. Mu MCP mwalowa anthu ambiri pakatipa koma mukumangokweza dzina la Mia lokha kumuopa eti? u President ochokera banja limodzi tatopanawo kani ndi umfumu?

 61. Mau omwe anayakhula bingu iweso ukubweleza iwe pitala u will never win in 2019, bingu anachita bwino term yoyamba koma iwe failed

 62. Manyazii bwanji Pitala?. Maloto a chumba amenewo. Ukuganiza kuti ndani akusangalala ndi ulamuliro wako?. Unyenyedwa ndiwe 2O19

 63. Boma ngati munaliona likuluza. MCP muziwafunsa aja anatisiya aja a chakwamba anadya one koma zinathera kuti

 64. makape nonse khalan chete mukundinyas,tizimvela inuo?komwe akudyela ndalama zaozo simukudyanao.tien tidkile 2019 bas.

 65. kodi galu ameneyu iye siwamulungu.nanga msonda DPP adagula pa bwa kkkkkkkkk APA zaoneka kuti DPP yapita motchipa kwamsonda pamenepo MCP yapita mokwera.

 66. In a free & fair elections Nyapapi will neva win.A Malawi anachangamuka pano,anatopa nd chitukuko cha pakamwa.Tione kuti october by election iyenda bwanji mostly ku lowershire ku

  1. iwe ndi wa mcp ndani sakukuziwa ma coment ako amakhaka otukwana ngati siye mamuna man nanga mcp angawine dziko pa central poka muziganiza bro

 67. Zinazi muzisyilako anawa aziyankhula bwererazo, nanga munthu wa nkulukulu zaka 77 nkumachita zinthu ngati mwana. komaaa!! a president and a proffessor for that matter, ndimaona kuti on his 77th birthday he will demonstrate maturity koma ashiiiii ngati kamwana ndithu, munthu wankulukulu believing in lies and fallacies.

  1. Hahaha eti munthu akuti ndi professor kuyankhula ngati mwana wa zaka ten.ndi chifukwa Malawi yasaukitsitsa ndithu ndi nkhalamba ngati imenei.

  2. I thought simumanveratu ma speech ake monga inu ana a zimbano , munvadi kuwawa. Kkkkkkk kumsuzumira neighbor kumeneko?

 68. No more nkhalamba ku state house, akanakhala wina akanangoti sindiima 2019 to avoid embarrasment. Malawi is not zimbabwe nkhalambayi ikapume.

  1. Unfortunately he does not have a strong competetor. Is somebody failed to manage a church with about less than 1mil followers, then he us failing to manage his party with about 4-5 million followers. Can he manage 17 million people? I daubt. Let’s wait and see how it goes.

  2. Iwe ndiamene ukuona ngati alibe competitor, mwiniwake akudziwa kuti he will face stiff competition in 2019. Ndi chifukwa chake competitor wake amamutchula pafupipafupi. Chakwera never failed to run the church, he was not fired. He made a choice kuti ayeseko ndale. Ena anapangaposo nhati achina dumbo leman, wilson ndomondo, mzomera ngwira kungoti enawa ndima mp zaupresident sanapangepo.

  3. Kaya Amakanika Kuyankhula He Z Stil Ur President And He Will Also Win In 2019 trust me on that one chakwera wil never be a president on this planet

  4. Kaya bola nzanu ali kale Ku state house, ndipo akupitilizaso 2019.winawe uzingobwebweta basii olo atani palibe chake chakwela trust me DPP,will carry the day!!!!!

  5. Azatulukako kumenekuja dzuwa likuswa mtengo. Ukaluza ngati pamakhalaso xcuse yokhalira ku state house, umangotuluka mwakachetechete.

  6. Rod Ine Ndi Wa Chelsea Iwe Wa Asernal Always On The Loosing Side Bwanji.If U Follow Politics Dpp Has A Big Following. Kodi Anthu Okalamba Ndiamene Amasamala Mudzi Amene Timafunsako Nzelu

  7. Sitikufunaso Anthu Otopa Kale Ife Nchifukwa Chake Akumaba Ndalama Za Boma Chifukwa Amadziwa Kut Ine Ndakalamba Kale,,,,,,, Usayimenso Jst Pack And Go Ku Thyolo

  8. Dpp 2019 Boma again !!!!! wina afube asafune remember 2014 chakwela analikuti nanga uyu Peter anali yani that time

  9. Mutha -rika,osusa Mutha Mau,mesa Big Late Man Alipo Mukati Siufumu Kut Alowe M’bale?Nkaona Ngat Muli Nd Bale Wanu Kt Alowe Mmalo Mwake Mungonena Mulibe Vision Vuto Ukamafuna Utsogoleri Umakukana,koma Umakana Umakusata,nonse Osusa Mukhale Macandidate 2019 Mukakhale Ku State House Tione Ngat Mungakambe Zanzeru Mwamva

  10. aaa zoonad a chewa mukavotere kamnyamata kanu ka chakwera kkkkkk angoni vp wathuwathu chilima…alomwe adad adadadadadad mcp probably nganganga ku oppostion no doubt about that,

 69. i think unali usanabadwe m,mene kamuzu Banda amaluza eti.? Vuto mkusayenda, Lupiya Banda analuza bwanji? Ngati iwe ukavotele dpp it doesnt mean kuti idzawina ayi. . Kamuzu anali muthu muthu osati izi aaaa awa…! koma analuza, ndeye munene izi? Aaaaaa. Ukamufuse Dr bakili Muluzi or Dausi about kamuzu. Aaaa ati petulo ehe!!! Kaya.

  1. kkkk ma project osalimba ngati Karonga-Chitipa road. Anthu akuona ndipo DPP ikulandira Red Card. PP inaluza bwanji? So shall DPP lose too.

  2. Ine I stay in Mangochi. Ndipo I have seen ka improvement. Mangochi – Liwonde road under construction. Then Mangochi Stadium, Mangochi Town hall, Water Tank, Mangochi Technical College . Of course some projects in progress. That’s why I say these will act as Campaign weapons during the Election. Ofcurse pali transformation atleast

  3. hahahahahah muziona 2019 peter wanuyu chitukuko chake chiticho chitukuko anapanga ndi nkulu wake osat iyeyooo chakwela 2019 bomaaaaaa

  4. A chikoko muli ndi maso inu come ku nzuzu kuno ,,odl cumpus ķu mzuni ikutheka;rumphi ttc ikutheka,saļima wàter project ikutheka,nkhatabay road strabag ikumenya,chitipa water project sawa group ikugaya!!ķođi inu muneña chani inu asayenda inu chaķweŕa wañuyo adzapangachani??adzambila pàti kkkķkk ķoma mulimbetuu??cancer ceñter nañga???àka tumbu onyela n’dàmbo munya 2019 dpp ikunyenyanidiii!!!

  5. kodi chitukuko sakupanga kumpoto kwanuko ife kwanthu kuno sadabwele mkomwe tikanena zachitukukocho nde ndi zero nde tikavotere dpp yatani kufuna kuti tisaukilebe mmene watinkhaulitsila nkulu ameneyumu

  6. komaso ku mpotoko olo mutaphatikizana nonse kuvotera ka dpp kanuka sikut mungawine nonse kumeneko ka population kanu ndi haif ya Dowa kkkkk

  7. Hahaha odzavota ndife anthu, kazipusitsanani nokhanokha.koma chilungamo ndichakuti M.C.P ikudzatenga boma..ngati simukuopa chakwera bwanji mwayamba kale campaign? Kodi ino ndinthawi ya campaign? Chi president chafundo ngati mwana hahaha professor oyankhula fundo ngati mwana wazaka ten.M.C.P ikutenga boma 2019 Lekani kulota anyapapi inu..

  8. A Stain Chikoko Mpaka Ife Agalu Kutukwana Anthu A Kongeresi Simuzatheka.Mwatukwana What Difference Does It Make Then Have You Become The Ruling Party Now. You Dont Knw Politics Wait Til 2019 Mpamene Uzaziwe Kuti Dpp Ndi System Ina Iweo Ndi Ka Mcp Kakoko Ka Tukwana Ukhala Choncho Ife Tikulamulira

  9. Kodi MCP kuwinako izadusa potani? Kkkkkkkkkkkkk muwafunse a chair ananena kale kuti palibe amafuna kubwelera m’mbuyo, pano ndi nthawi yopita chisogolo za MCP iwalani ndi maloto chabe amenewo. Mbiri ya MCP inaipa kale-kale panopa ngakhale atachapila boom singaele kapena kusukika ngakhale pang’ono

  10. But If He Is Not A Leader Sangalamulire Olo Mulungu Akutikonda. God Loving Us All Does Not Mean We Can Rule Mw Whenever U Feel Like Becoming A Leader.

 70. Tanthauzo lapinyolo lavuta apa,Sidik Mia waphwanyitsa ena mitu apa,inu tadzingoamwetsani anthu bibi mu LL mo

 71. Sime of these comments are not worthy of a whole Head of State. Leave some of these things to loud mouthed Regional Governors or whatever they are called. Honestly such utterings zinayamba witj the likes of Charles Kamphulusa Davies Kapito Morris Kachimbwinda and now the new kid on the block Jeffrey….come on give us a break and start talking about policy.issues!

 72. ndipo osatinso kunyenya mwake kongoyelekeza aaaa iiii, kunyenyelatu aganize bwino analowa zolakwika kuthawa kusamala nkhosa za mulungu, mulungunso akumuyang’anila kumbali bwana peter tinyenye basi osawasekelela

  1. Udziwe ichi Lupia ku zambia adali president koma adaluza movetsa chisoni ndiye kuli bwanji Nyapapi wapakamwa pobwafukayu?

  2. Zandalezi sikweni kweni,koma iyiyi yandifika,achakwelatu akusakaniza zithu akapanda kutengazithu bwino ziwasokonekela mulengi akakwiya nazo,mbusa akhala bwanji mmsongoleli wa dziko,ndimmene ayakhulila a lucias mu?

  3. hahaha zaka zino munthu kumalimba mtima kumat ine wa mcp,kkk olo atatenga doom kundiyika kamwa na mcp yokha sindigakavotere and mcp sizalowaxo boma believe me

  1. tonse tili apa ndakapolo oti sitikudziwa kut zimakhara bwanj kwathu mkutenga ma ziphaso zovotera mkukayima pa line kuvutika ntchito yot ena agwira kale kutereku vote ya winawe nd ya peter kma sungadziwey

  2. If you trying to say dat boma silimaluza what do you mean? Ask kughana ngati sukudziwa kumayenda amwene osamangokhala malo amodzi in Ghana opposition is the one who is rulling now

  3. Ndiye tigwire ziti mukuti boma LA pp lidaluza Kaganizani ngati amalawi , with this president this nation won’t develop any more

  4. Boma limaluza ,chipani cholamula chaku America chimene amayendetsa brack Obama chinaluza,Ku Zambia chipani cholamula chinaluza,Ku Ghana chipani cholamula chinaluza Ku Brazil chipani cholamula chinaluza ndiye bwampini iwe ukuti chiani?

  5. kumbali yanga ndale za ku malawi kuno ndimaona ngat zimasiyilanako ndi za mayiko ena,fanz kuno ndimaona ngat imakonda chipani chifukwa cha mtumdu wawo komaxo chigawo chomwe akuchokera kona dpp ili ya mphamvu kumwera mcp pakati pomwe nowdays kumpoto pp ikumaoneka ngat ndi ya mphamvu kumeneko,another thing ndichakut chiyengo chimachuluka kwambiri so pa chisakho chipani chili boma zimaone kut chimakhala ndi upper advantage than anzawo JB uja anagofoyira yekha kuyiwerenga kona akadandaula kut chisakho chaberedwa,believe me dpp izawinaxo

 73. Anyenyeni kwinaku mukunyenya dziko lathu lokongola ,nanunso mamilion adzapezekanso kunyumba kwanu mukadzayamba ulendo wotseka maso,tinyenyeni tinazolowela kudyeledwa ndi anthu opanda history.

 74. KKKKK, KOMA ABALE PENA PAKE TIDZILANKHULA ZA MZELU MUNTHU UKANJENJEMELA BWANJI ULI M’BOMAKALE. TAMAKUMBUKILANI INU 2014, APITALA ANALI AOPOSITION OLAMULA ANALI A PP KOMA ANATEMBENUZA APP KUKAPEZEKA KUNJA MKULUYU M’BOMA ZINACHITIKA PAMENE PAJA AMAI MPAKA KUSOKELA. ACHAKWELATU ALISO POMPO.

 75. pali zitsiru zina zawanthu unzimva DPP 2019 m’boma… kaya kumakhala kusavala chovala chamkati. inu DPP nchonyadila? mumanyadila coz ndi mbuzi xa anthu. nde pali asasamba ena a MCP. awa nde dziko sazalamulira mpang’ono pomwe kumangozivuta Chaka chilichonse. mukuona ngti anthu angapange xoti mutenge boma? nyau zingalamulire dziko? zosatheka. achewa pezani china chochita. ati MCP. mumawina pa Facebook basi akanganya inu

 76. mmm muthalika chikumukhudza ndichani pa khani za chipani cha mcp? Ndi member wa mcp iyeyo? Mmmm wakalambadi uyu eti? Useless. Man. Akuwopa chani ?

 77. Musathe mau bwana sionse omwe akukondwela ndiusogoleri wanu ziko muliephela kulamula mukathila phula nsewu kwa 1kiromitre mukumadziguguda pantima kkkk ine olo atandithila doom kamwa yaine yokhayi vote simuzainukha

  1. ine oro atandithira doom mkamwa oro kufuna kundiviika mmadzi ozizira koma ndikunenesa sindidzaloraso kut ndalama yanga ya msokho chaponda kut apondeso,sindidzalora kukhara ku chanco for 8 years for a degree,munthuyu ukamakura umabweleradi ku chimwana ,u make decisions ngat mwana ndaziona ine ndili ndi umboni mu dziko la malawi..pepani a Lovemore bwana anuwo sitimawafiraso

 78. Judas,Jonah koma munthu wa mulungu sakuyenera kulowelera ndale chifukwa a ndale akasowa nzeru amathangira ku mpingo kukafunsa koma apa wakumpingo alowa ndale tikafunsa ndani?

 79. Koma ndizoona kodi Mia akukalowa muchipani kodi pakati pa Mia ndi Mcp amene akanapanga hire Lucius akanakhala ndani? Chopani chapita basiiii

 80. Pitala Saakunama! Chakwera Wagulitsa Chipani Kwa Bwana Mia! Kkkkkk Ndidzakumbukikira Mawu A John Tembo Oti Chakwera Ndi Nkholokolo

  1. nde misalayo imeyi! nanga palinxo fundo zoti munthu wanzeru zake angamat ndchilungamo apa? what can Malawi benefit from your lunatic’s President’s saying? you both deserve to be nincompoops, morale rotten guys!

Comments are closed.