Mayi agwilila nyamata wa zaka 14

192

SexApolisi mu boma la Kasungu atsekela Mayi Rosemary Banda a zaka makumi asanu ndi mphambu zinayi (54) kamba kogwilila mwana wa zaka 14.

Malinga ndi oyankhulila a Polisi mu Boma la Kasungu, Bambo Harry Namwaza, mayiwa adachita zachipongwezi chaka chomwe chino.

“Iwo anapita kukacheza kwa anzawo pakati pa usiku. Atamaliza, anapempha kuti mnyamata mmodzi awapelekeze,” anatelo a Namwaza.

Iwo anati mnyamata amene anasankhidwa kuwapelekeza mayiwa anali mwana wa zaka 14.

Ali munjila, mayiwa anatembenuka ndi kumbwandila mwanayu ndi kumukakamiza kuti achite nawo zopusazo.

Mnyamatayi atafika kwawo anaulula ndipo mayiyu watsekeledwa kudikila tsiku la Mulandu.

Share.

192 Comments

 1. Mayiwo Mwina Anatopa Komaso Anyamata Azaka 14 Akusiya Zimimba Mamidzimu Mayiwo Atulusidwe Ngati Amangidwa Atulusidwe Ifeso Tinaziyamba 14 Yomweyo

 2. What I Know Is That Sooner Or Later You Will See Her Walking Freely.Apolice A Ku Malawi Atamuchita Zina Ndi Zina.Ndende Za Kumalawi Ndi Za Amuna Osauka Basi.Mahule,amai Ndi Olemera Ndi Afulu.I Rest My Case.

 3. aliyese amachimwa koma eeesh zaonjeza nde mwana wazaka 14 simwana amaziwa chomwe amachita afusidwe kaye asanamange agogowo,komaso azimai mwayambazi ndi mbola,ngatipamayabwa osangoikapo kandulobwa kusiyanandi uve achita agogou,zachisoni,tizingopemphela kuti enafe zitichoke

 4. Kkkkkk Mufuna Kundiwuza Kt Mnyamatayo Samatopola ? Ogwililira Pamenepo Palibe Coz 14 Yr Old Ngat Anali Pamwamba Nde Kt Nayeso Amafuna,,, Mzimayiyo Mtayen Cfkwa Anthuwa Ndi Nyere Inasawutsa Onse

 5. Kkkkkkkkkk Zingatheke Bwanj Mwamna Kugwililidwa Ndi Nkaz ? Kutheka Amaafunanso Amayiwo Nchfkwa Anapanga Zimenezo . Pot Anaapeza Nchfkwa Pabwela Maw Oti Amgwililila

 6. Mmmh koma chinthakati chimenechi chopusa kwabasi kugwilira mwana choncho achimange chiolele kundende konko chimfiti cha mai chandikwiyitsa kwabasi mwanayo ndekuti analibe mphamvu mmh

 7. mmmmm sindikwanitsa kuika ndemanga zindibvuta ndingachimwe nazo izi tili mmasiku womaliza chongofunika kupemphera basi.dziko lapansi lawonongeka ndizambiri chimodzi mwaicho chiwanda chafika ndichogwilira ana ang,ono.

 8. Amalawi tili nivuto chibwezi chamzanthu timachinyodola aniwake amagwilizana zochita inu mwaonjezela zaka mzimayi ameneyo atuluke alibe mlandu ayi.bwanji kumalawi mumakokomeza nilandu yogonana koma yaumbava ayi.mulinivuto agalu inu apolice.mwana uyu chaponda bwanji apa simumumanga.

 9. Always confused with such case. Mkazi ngakhale iye alibe chilakolako ukhonza kumugwililila, koma mwamuna popanda maganizo ndi thupi lake kuvomeleza nzosatheka olo pang’ono. Ndiye amuna amagwililika bwanji? Kodi mkati molimbana momwemo chilakolako chimazambatuka? Nanga wokugwilililayo amamaliza iwe ukunyinyilikabe? Kapena mkatikati momwemo maganizo ako amafokesedwa ndi kukula kwa chilakolako chomwe wakupasa omwe amapangisa kuti uzivomeleze, zomwe pambuyo pake umazindikila kuti si zomwe umayembekezela then umakaulila?
  Ndithandizeni kumvesa zinthuzi guys.

 10. Palibe chifukwa chomangidwira munthu apa ana ena azaka 14 akumapereka mimba m’midzi mwathumu kungoti mwina gogoyo anali opanda ma looks a bhoo

 11. A boss said to his secretary “I want to have SEX with U. I will make it very FAST. I’ll throw R1000 on the floor, by the time you bend down to pick it I’ll be DONE.” She thought for a moment then called her boyfriend and told him the story. Her boyfriend then said 2 her, do it but “Ask him for R2000, pick up the money very fast he wouldn’t even have enough time to undressed himself.” So she agrees. Half an hour goes by, the boyfriend decides to call his girlfriend, he asks, “what happened?” She responds,”The Bastard used COINS, I’m still PICKING and he is still fucking!!! Boyfriend fainted..
  Make someone laugh as well! Share!!!!!!!!!!

 12. In my village when a pastor dies… We pray all night till the next day. When a drunkard dies, we drink all night till the next day. Yesterday a prostitute died…….. We are awaiting for the village elders to decide. Meanwhile am on my way to the village.

 13. akuenela kulandla chigamulo ngat cha munthu wammuna,regardles of her age n appearance.kufuna kumpasa matenda mwanayobas!! shame on u!