Tulani pansi – alangizi a Mutharika auzidwa kamba kobisa matenda a Tate wa dziko lino
Alangizi a mtsogoleri wa dziko lino alamulidwa kuti atule pansi udindo wawo ati chifukwa akhala akubisa matenda a mtsogoleri wa dziko linoyu. Izi zanenedwa ndi mtsogoleri wa chipani cha Umodzi a John Chisi. A Chisi… ...