Malawi Police officers in the lakeshore district of Nkhotakota are keeping in custody 36 year-old Frank Kampala for being found in possession of Indian hemp which is locally known as Chamba.
According to Nkhotakota Police Public Relations Officer Williams Kaponda, police in the district mounted an ad hoc roadblock at Mkaika Trading Centre and later a Lakelands passenger bus travelling from Dwangwa to Blantyre with passengers on the board stopped at the roadblock.
“Upon conducting search in the bus boot, police found two big black travelling bags loaded with Chamba,” Kaponda said.
When the police officers questioned the driver they found that the bag belonged to Kampala.
The law enforcers seized the illicit drug and the suspect will appear in court soon to answer the charge of being found in possession of Chamba which is an illicit drug.
The suspect hails from Ndinda Village, Traditional Authority Kalumo in Ntchisi district.
Munthu kugulitsa chamba ndikuopa kuba koma a police akumumanga, wokhudzidwa ndi cash gate akutetezedwa ndi president, a Malawi tiyeni ku Capital Hill kukaba ndalama za boma, president atiteteza kusiyana ndi kugulitsa chamba, a police apezerapo ntchito
Palibe chifukwa chom’mangila munthu yapa
NDIYE ZIKATELE CHAMBACHO CHIMAPITA KUTI? Popeza apolisi muma suta chamba ndi chifukwa chiya mukumawa gwila ali ndi ogulisa chamba?
Zolimbana ndi Herb… ndi Zausilu
Shame!!!!!!2 that man,Azake timangwilizana kaye ndi a police omweo timango achuna 10G timadutsa nacho,Ngati apapa ndikudutsa pa Benga ndangonyamulako 5 bags basi apa Kaphatenga ndawachuna kale andiuza kuti ndikadutsepo Usiku,Nde ndiima kaye Mwasiyasiyama.Ine ndimagulitsila pa Kr Ochifuna azindipeza ndilinacho chochuluka,Koma kuyambila pa 1 mwezi ukubwelau tikweza mitengo,Zikomo ma custorms nose
Ndikufuna 1000kg man
Ndili ndi Chosakwana nde ndiyankhulane ndi wa Police wina wake alinacho,Ndikuuzani
apolice akumalawi kunvetsa chisoni Hee mbuli zeni zeni.
apolice akumalawi kunvetsa chisoni Hee mbuli zeni zeni.
Kukhala m’malawi ndikulimba mtima
U Malawian Police Motherfuckerz.Moti Mukamange Joyce Banda Uko,anaba Chuma Cha Dziko Nde Mukamanga Munthu Coz Of His Own Property,zapantumbo
A police akumalaw panyapanu kwambiri,ndiye kut amene amgwidwa mophweka ndionyamula chamba?.komaso mbuz ndiokuphuztsaniyo coz adakuphuzitsan topc imodziyokha yakagwlidwe kachamba,kumatako kwanu.
Awunsilu azigwanyawa aise
Mboli zao ameneo saziwa kuti ife timatchuka mmaiko anza2 wa chifukwa cha chamba
free him & legalise it
God is the solution.
why arresting him!!! kungokhomele basi
a woz n court….dzulo dzuloli ine kudabwa court magestrest akundifusa kut mwapezeka ndmatumba achamba ten
a woz n court….dzulo dzuloli ine kudabwa court magestrest
Come n arest mi cz hv got million ov bags.
Malawian hemp
stop arresting people for stupid things, am sure is too much job for you to do. like protecting albinos, find cash gAte thief, arresting Kamlepo etc
Isn’t is INDUSTRIAL HEMP?
Umbuli wa a Malawi Malo mopanga Zina kulimbana ndi zomera kkkkkkkk Kma kuopa kumanga wopha ma albino shame
makwala awa amutu,dzina lake ndi #mangwelalala mutuluseni please,mukumuchedwesa timadalira omwewo,popanda amenewo sizinga chitebwino kkkk.
agaluso inu eti? mesa munkati mwayamba ulimi wa chambaso? chikanapezeka ndiwa m’boma simukanamumangatu inu!!
My name is Musonda Kaluwe and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.
Peter Tosh-LEGALISE MARIJUANA!
so what,,,,,
funk the police
Kkkkkkkkk koma zinazi munthu asanyamule mankhwala zakuti ndi chamba mukudziwa ndinu kwa ife ndi mankhwala
Why? I thought it’s legalised? So confusing.
even in malawi u call it chamba,we do the same here in zambia.
M frm South Africa whr can I get this chamba?
i hared that there is soweto there,go there u will find it.in local we call it chamba that is in malawi and zambia but according to english it is called cannabis and marijuana okay?
Mutuluseni ndi osalakwa chifukwa boma linavomereza za kusuta public
Kodi kumaphunziroko mmangophunzira kagwiridwe kachamba ndi vacab basi???
Mbuzi za apolisi
Am the chambaologist…..
Pipo are getting rich, , chifukwa cha weed…….inu mukumanga ….manja ndi anu?
Mbuzi police ,
Ur economy, let de man go free
Kodi mesa azigulitsa chamba-cho kuma company..nde why arresting him? Nde zachamba zimenezo a police
So wat?mukalanda mudzikagulitsa ndinu,zachamba basi!!!!
Eish here we go again ndiye a police ndi adziwa ine ndende zakumalawi kuno kudzaza ndi ati ogwililira ogulutsa chamba ndi ongomupeza panseu akuchoka kumowa chosecho mbamva zikuluzikulu zingonjoya eg a cash gate opha albinism oba magalimoto eish my Malawi
Eish here we go again kodi apolice akuno kwathu ntchito ikhalira yogwila anthu
Kodi mesa munavomeredza kuti tidzilima nangaso bwanji kodi mufuna muzigulitsa nokha
Masuleni mnthu agalu inu
Zawuchiru
Chamba chimaoneka chomchi?
Makobidi amenewo
Imeneyo ndi mbewu cz Boma linavomereza kut amalawi azilima chamba …Xo xet hm freeee!!!!
mucyilen chambacho ..bwanj cod apolic anamachende inu.
release the guy,he just making an honest living
ndye alakwa chani palibe chifukwa chomumangila munthu yu coz Malawi depending on agriculture, ndechambacho sichili gulu la Agriculture.
Marijuana is not a drug.
Abwampini a polisi inu chambacho ndi chake sanabele munthu, set him free right now kupondeza aumphawi baxi
Malawis green gold
free the Ganja sale sanabe kapena kupha..
why why the product is already legalised by gorvernment police too harsh
So what??? Failing to arrest those scumbag ministers!!!