Malawi Police officers in the lakeshore district of Nkhotakota are keeping in custody 36 year-old Frank Kampala for being found in possession of Indian hemp which is locally known as Chamba.

According to Nkhotakota Police Public Relations Officer Williams Kaponda, police in the district mounted an ad hoc roadblock at Mkaika Trading Centre and later a Lakelands passenger bus travelling from Dwangwa to Blantyre with passengers on the board stopped at the roadblock.
“Upon conducting search in the bus boot, police found two big black travelling bags loaded with Chamba,” Kaponda said.
When the police officers questioned the driver they found that the bag belonged to Kampala.
The law enforcers seized the illicit drug and the suspect will appear in court soon to answer the charge of being found in possession of Chamba which is an illicit drug.
The suspect hails from Ndinda Village, Traditional Authority Kalumo in Ntchisi district.
60 thoughts on “Man in for marijuana”
Comments are closed.



Munthu kugulitsa chamba ndikuopa kuba koma a police akumumanga, wokhudzidwa ndi cash gate akutetezedwa ndi president, a Malawi tiyeni ku Capital Hill kukaba ndalama za boma, president atiteteza kusiyana ndi kugulitsa chamba, a police apezerapo ntchito
Palibe chifukwa chom’mangila munthu yapa
NDIYE ZIKATELE CHAMBACHO CHIMAPITA KUTI? Popeza apolisi muma suta chamba ndi chifukwa chiya mukumawa gwila ali ndi ogulisa chamba?
Zolimbana ndi Herb… ndi Zausilu
Shame!!!!!!2 that man,Azake timangwilizana kaye ndi a police omweo timango achuna 10G timadutsa nacho,Ngati apapa ndikudutsa pa Benga ndangonyamulako 5 bags basi apa Kaphatenga ndawachuna kale andiuza kuti ndikadutsepo Usiku,Nde ndiima kaye Mwasiyasiyama.Ine ndimagulitsila pa Kr Ochifuna azindipeza ndilinacho chochuluka,Koma kuyambila pa 1 mwezi ukubwelau tikweza mitengo,Zikomo ma custorms nose
Ndikufuna 1000kg man
Ndili ndi Chosakwana nde ndiyankhulane ndi wa Police wina wake alinacho,Ndikuuzani
apolice akumalawi kunvetsa chisoni Hee mbuli zeni zeni.
apolice akumalawi kunvetsa chisoni Hee mbuli zeni zeni.
Kukhala m’malawi ndikulimba mtima
U Malawian Police Motherfuckerz.Moti Mukamange Joyce Banda Uko,anaba Chuma Cha Dziko Nde Mukamanga Munthu Coz Of His Own Property,zapantumbo
A police akumalaw panyapanu kwambiri,ndiye kut amene amgwidwa mophweka ndionyamula chamba?.komaso mbuz ndiokuphuztsaniyo coz adakuphuzitsan topc imodziyokha yakagwlidwe kachamba,kumatako kwanu.
Awunsilu azigwanyawa aise
Mboli zao ameneo saziwa kuti ife timatchuka mmaiko anza2 wa chifukwa cha chamba
free him & legalise it
God is the solution.
why arresting him!!! kungokhomele basi
a woz n court….dzulo dzuloli ine kudabwa court magestrest akundifusa kut mwapezeka ndmatumba achamba ten