30 million yapelekedwa kwa achinyamata 30 kuti akachitire malonda osiyanasiyana
Achinyamata okwana 30 dzulo alandira ndalama zokwana K1 million aliyense kuchokera kwa m'modzi mwa anthu ochita malonda m'dziko muno, Triephornia Thompson Mpinganjira. Achinyamatawa alandira ndalamayi kuti akayambire malonda osiyana-siyana komanso kupititsa patsogolo malonda awo pansi… ...