A Malawi kudzaipatsa moto! Akusonkha ndalama yoti Mai Mbambande akamubwezere Triephornia Mpinganjira
Ayambe kumbuyoko/Ayambe kumbuyoko kudzapeleka aaa/tiyeni tonse tikapeleke: Iyi ndi nyimbo yomwe akuimba anthu omwe alowa gulupu la pa ‘WhatsApp’ lomwe a kuti likusonkherana ndalama yoti Mai Mbambande akabweze kwa Triephornia Mpinganjira. Zoonadi, mbuto ya kalulu… ...