Nyimbo udayimba ndi Mafo ilikuti? Amalawi afunsa Gwamba
Amalawi adabwa ndikuchedwa kutuluka kwa Nyimbo yomwe Katswiri wachamba cha hip hop Gwamba adaimba ndi Madala Mafo mu chaka cha 2020. Gwamba adalonjeza mtundu wa Amalawi kuti ausa Mafo kwa akufa muchakachi. Ndipo adatsimikiza izi… ...