Mneneri Phiri wapezeka olakwa pa mlandu ochita za akuluakulu ndi mwana wake
Bwalo lamilandu ku Mangochi lapeza olakwa m’neneri Christopher Phiri wa mpingo wa Supernatural Embassy pa mlandu oseweretsa malo obisika a mwana wawo wa mkazi zomwe akuti zinali ndi kuthekera koti anakagonana naye. Apolisi kumapeto kwa… ...