Kusamvana kunabuka pamalo omwetsera mafuta
Kusamvana kunabuka lero m'mawa uno pamalo ena omwetsera mafuta a Petroda pa Kamuzu Road m'boma la Salima pamene mkulu wina amakana kusuntha galimoto lake. Mkulu wina yemwe amaonetsetsa kuti zinthu zikuyenda mwa dongosolo anapempha bwana… ...