Kalindo adzudzulidwa kamba kofuna kuti Chizuma achotsedwe ntchito
Anthu ena m’dziko muno akupitilira kudzudzula zomwe wayankhula Bon Kalindo posachedwapa kuti mkulu wa bungwe lothana ndi katangale la ACB, a Martha Chizuma, achotsedwe ntchito. Nkhaniyi ikudza pomwe posachedwapa bwalo la milandu mu mzinda wa… ...