Luanar ikuyesa mbewu ya chimanga chopilira kumbozi
Pali chiyembekezo choti zaka ziwiri zikudzazi, dziko la Malawi litha kukhala ndi mbewu yachimanga chopilira ku mbozi komaso mavuto ena pomwe sukulu yaukachenjede ya LUANAR yati ntchito yoyesa mbewuyi ikuyenda bwino. Akatswiri a sayansi pa… ...