Msonkhano ku Saudi Arabia walepheleka, Chakwera apitabe?
Pomwe mtsogoleri wa dziko lino analongedza kale zovala kuti anyamuke lero lachitatu kupita m’dziko la Saudi Arabia ndi anthu osachepera 70, msonkhano omwe amayenera kupitira wa Africa-Arab Summit walepheleka. Lachiwiri sabata ino boma linalengeza kuti… ...