PAC yapempha a Chakwera kuti achepetse chiwerengero cha nduna komanso alangizi

Advertisement
Malawi President Lazarus Chakwera

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, apemphedwa ndi Bungwe lotchedwa Public Affairs Committee (PAC) kuti achepetse nduna zake komanso chiwerengero cha azilangi ake ndicholinga chofuna kupulumutsa chuma pamene dziko lino lakutidwa ndi mavuto osiyanasiyana azachuma.

Bungwe la atsogoleri a mipingowa linaykuonongeka mdziko muno kamba kakuti mtsogoleri wadziko linoyu amachita ziganizo mochedwa komanso sakhazikika muzochitika zake.

Mwazina, bungweli linayamikiranso mtsogoleli wadziko linoyu kamba ka zitukuko zosiyanasiyana zomwe a Chakwera akupanga monga kukonza misewu.

Bungwe la PAC limayankhula izi ku mkumano omwe unaliko ndi mtsogoleri wa dziko linoyu.

Wolemba: Ben Bongololo

Advertisement