
Timangofuna tikuoneni – Khuda wati banja silinathe
Nyimbo ya ‘Atambwali okhaokha’ ya Gibo Pearson ndi yomwe katswiri wosewera mpira wamiyendo, Khuda Myaba, akumvera pano kamba koti zoti banja lake latha ndi nkazi wake Enlecio, zinali nthabwala chabe ndipo wati iyeyo anakonda hule… ...