Chakwera asiya Malawi pamoto wa ku Iguputo
Ulendo wa ku Kanani walephereka. Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wasiya Malawi akulira ndikuphula njerwa za moto. Chakwera yemwe anayenda mwakachetechete kuopa kuwowozedwanso ku Lilongwe akuti wafika bwino ku Iguputo. Lachisanu, a Chakwera anawowozedwa… ...