Munthu ndi m’chemwali wake amangidwa kamba kochita chiwerewere pachibale
…mpaka anabeleka ana awiri Zina ukamva, thupi lonse limagwidwa nyetsi. Munthu ndi mlongo wake amangidwa kwa chaka ndi theka zitadziwika kuti amazembelana mpaka kufika popatsana mimba kawiri ndi kubeleka ana. Malinga ndi nyuzipepala ina ya… ...