Winiko

Kalindo watuluka pa belo

Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lapereka belo kwa Bon Kalindo yemwe anamangidwa pomuganizira kuti anafalitsa uthenga omwe unali ndikuthekera kobweretsa chisokonezo okhudza ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a… ...