Mwana wakhanda wapezeka atafa mumtsinje wa Likangala
Mwana wakhanda wamiyezi yosachepera itatu yemwe mai ake sakudziwika wapezeka atafa mumtsinje wa Likangala mu Mzinda wa Zomba. A Auzious Chimalala omwe amakhala m'mudzi mwa Chilupsa mu Mzinda wa Zomba awuza Malawi24 kuti ana ena… ...