Mulandu wa sing’anga ogwililira atsikana anai uzapitilira pa 2 May
Bwalo la milandu ku Zomba lizapitiriza mwezi wamawa kumva mulandu wa sing'anga wina Malizani Pawoneke Salizeni yemwe akumuganizira kuti anagwililiraatsikana anai achichepere osakwana zaka 17. Malizani Pawoneke Salizeni yemwe ndiwa zaka 23 zakubadwa adapalamula mulanduwu… ...