Vera wa zaka 10 ku Balaka akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali
Vera Kadwale wa zaka 10 yemwe amachokera m'mudzi wa Ngomano, Mfumu yaikulu Chimatiro M'boma la Balaka ndipo salankhula komanso kuyenda akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali. Vera akukanika akusangalala ndi maufulu osiyanasiyana omwe ana… ...