Ndine okwiya kwambiri, mudzayankha mukundipangazi – walira mokweza Norman Chisale
…wati anthu akuzuzika kwambiri pano kusiyana ndi nthawi ya DPP …wati sadzawakhululukira a Steven Kayuni Wachitetezo wamkulu wa mtsogoleri wakale wa dziko lino Peter Mutharika, a Norman Paulos Chisale sanafuna kusunga zakukhosi pomwe awulura kuti… ...