Zongotipeza kumene: Ngozi inaso ku Blantyre
Patangotha maola ochepa anthu akukamba zangozi yomwe yachitika m'bandakucha lero, ngozi ina yachitikaso mu mzinda wa Blantyre. Malipoti omwe tsamba lino lapeza akuti galimoto ya mtundu wa thilaki inaduka mabuleki ndipo inaomba galimoto zina zomwe… ...