Mayiko onse a padziko lapansi akusilila Malawi – watelo Mutharika
A Malawi ati muziyenda mapewa mmwamba, tukumutukumu, uku mozipopa ngati finye chifukwa pa dziko lonse lapansi nkhani ndi ya Malawi. Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika wati anthu a pa dziko lapansi akuyang’ana ndi… ...